Post Predictions & Updates

Login with Facebook to post predictions, updates & live scores

Tue, 19 Feb - Mon, 25 Feb 2019
Tuesday, 19 February 2019 CAT (UTC+2)

Osewera yemwe amasewera kutsogolo mu timu ya BE FORWARD Wanderers chaka chatha, Peter Wadabwa, ali ku Mozambique komwe akuyang'ana timu yoti asewere.

19 Feb 05:41
~Admin User

Otsatira timu ya Wanderers ati ndi okhutira ndi m'mene timu yawo yachitira pa msika pogula osewera ku matimu ena.

Mlembi wa masapota wa BE FORWARD Wanderers, Sam Mponda, ndiye wanena izi.

19 Feb 05:51
~Admin User

Akuluakulu ena oyendetsa matimu m'chigawo cha kumwera ati ganizo loti timu yomwe yatuluka mu Super League isamabwelere ku ligi ya ThumbsUp Premier Division silabwino.

19 Feb 06:05
~Admin User

Otsatira timu ya Wanderers ati akufunitsitsa timu-yi itatenga chikho cha TNM Super League komanso kuteteza FISD Cup chaka chino.

Mlembi wa masapota wa timu-yi, Sam Mponda, ndiye wanena izi.

19 Feb 06:13
~Admin User

Ligi ya m'chigawo cha kumpoto ya SIMSO ipitilira kulandira ndalama zochepa kuyelekeza ndi ma ligi ena mdziko muno.

Izi zikutsatira kusakambapo kali konse kuchokera ku sponsor wa ligi-yi.

19 Feb 06:26
~Admin User

Timu ya mpira wa miyendo ya dziko lino ya Malawi Under 23 lero masana isewera masewero ake oyamba mdziko la Belgium ndi STVV. Timu ya dziko lino-yi inachita zokonzekera zake kukonzekera za masewero-wa.

19 Feb 06:44
~Admin User

Silver Strikers will start 2019 season preparations today, Tuesday.

Club officials have confirmed about the development.

19 Feb 08:51
~Admin User
#WorldFriendlies
  STVV 3 - 1 Malawi U23
 18' Kinoshita, 41' Mmaee, 72' Thallyson - 82' Juma Yatina 
3:30 pm Stayen
   
 
FT: 3-1 (18' Kinoshita, 41' Mmaee, 72' Thallyson - 82' Juma Yatina) 
Picture
 
Prediction 1-2 
Picture
 
Malawi starting line Rabson Chiyenda Hadji Wali Denis Chembezi Charles Petro Isaac Kaliyati Chimwemwe Idana Levyson Maganizo Mark Fodya Peter Banda Batson Chikayiko Hassan Kajoke 
Picture

Timu ya dziko lino ya osewera achisozera ya Malawi U23 yagonja masewero ake oyamba ku Belgium ndi zigoli zitatu kwa chimodzi.

Malawi U23 imasewera ndi STVV

19 Feb 18:56
~Admin User
Wednesday, 20 February 2019 CAT (UTC+2)

Timu ya Silver Strikers yayamba zokonzekera zake za 2019 season dzulo mu mzinda wa Lilongwe.

Kwa nthawi ku timu-yi kunali kukokana-kokana pa anthu omwe ayendetse timu-yi chaka chino.

20 Feb 05:12
~Admin User

Executive Committee yatsopano ya Silver Strikers lero ikumana ndi Board of Trustees ya timu-yi kukambirana m'mene ayendetsere timu ya Silver Strikers chaka chino.

20 Feb 05:23
~Admin User

New Executive Committee at Silver Strikers:
Chair: Peter Chando,
Vice: Alick Tahuna,
GS: Laurence Yobe,
Vice: Innocent Kadammanja,
Treasurer: Judith Kachimanga,
Vice: Patrick Mbiliyakula.

20 Feb 05:28
~Admin User

Mkulu woyendetsa ntchito za Nyasa Big Bullets, Fleetwood Haiya, wati zokonzekera zonse za bonanza yomwe akonza kumayambiliro a mwezi wa March zili mchimake.

20 Feb 05:48
~Admin User

Bonanza yomwe timu ya Nyasa Big Bullets ichititse, padzakhala matimu anayi, awiri ochokera kunja kwa dziko lino, ndipo kuno ku Malawi izakhala Noma ndi Bullets.

20 Feb 05:50
~Admin User

Timu ya Malawi Under 23 lero masana isewera masewero ake achiwiri mdziko la Belgium ndi PSV.

Timu-yi inagonja masewero ake oyamba dzulo ndi zigoli zitatu kwa chimodzi pomwe amasewera ndi STVV.

20 Feb 06:31
~Admin User
#WorldFriendlies
  PSV Eindhoven vs Malawi U23
3:00 pm
   
Monday, 25 February 2019 CAT (UTC+2)
#WorldFriendlies
  OHL vs Malawi U23
3:00 pm
   
Tuesday, 26 February 2019 CAT (UTC+2)
#WorldFriendlies
  KRC Genk vs Malawi U23
 
   
Wednesday, 27 February 2019 CAT (UTC+2)
#WorldFriendlies
  Roda JC vs Malawi U23
2:30 pm
   
Friday, 01 March 2019 CAT (UTC+2)
#WorldFriendlies
  Patro MM vs Malawi U23
7:00 pm
   
Saturday, 02 March 2019 CAT (UTC+2)
#WorldFriendlies
  SP Hasselt vs Malawi U23
3:00 pm
   
Friday, 08 March 2019 CAT (UTC+2)
2019 CAF Champions League (3)
Constantine vs Club Africain; Orlando Pirates vs Platinum; Esperance vs Horoya;  
Saturday, 09 March 2019 CAT (UTC+2)
2019 CAF Champions League (4)
Vita Club vs Al Ahly; ASEC Mimosas vs Wydad Casablanca; Mamelodi Sundowns vs Lobi; Saoura vs Simba;  
Saturday, 16 March 2019 CAT (UTC+2)
2019 CAF Champions League (4)
Platinum vs Esperance; Horoya vs Orlando Pirates; TP Mazembe vs Constantine; Al Ahly vs Saoura; Lobi vs ASEC Mimosas; Wydad Casablanca vs Mamelodi Sundowns; Simba vs Vita Club;  

Updates

19 Feb 05:41
~Admin User
19 Feb 05:51
~Admin User
19 Feb 06:05
~Admin User
19 Feb 06:13
~Admin User
19 Feb 06:26
~Admin User
19 Feb 06:44
~Admin User
19 Feb 08:51
~Admin User
19 Feb 18:56
~Admin User
20 Feb 05:12
~Admin User
20 Feb 05:23
~Admin User