Login with Facebook to post predictions, updates & live scores
Cristiano Ronaldo is yet to resume training with Manchester United amid speculations that he is leaving the club this summer.
According to the club, Ronaldo is abstaining from the training due to personal reasons.
But the Portuguese star has made it clear that he wants to leave the club during the summer.
Meanwhile, no club has made a bid or showed interest in signing Ronaldo.
REPORTS| AC Milan are interested in the services of Chelsea star Ziyech.
At the moment, negotiations are ongoing between Milan and Chelsea to reach an agreement.
Barcelona star Ousmane Dembele is expected to extend his stay at the club.
According to the club President, they are in talks with the player regarding his contract.
President Laporta said "There is still no change/update for Ousmane situation,".
CONFIRMED| Former Tottenham Hotspurs and Wolves Manager Nuno Espirito Santos is the new Al Ittihad Manager.
Santos has signed a 2-year contract until 2024.
Eu so big fans de big bullets fc
Timu ya Blue Eagles ikupitilira kudandaula ndi momwe bungwe la Super League of Malawi (Sulom) ikuyendesera ligiyi maka poika masewero.
Malingana ndi Blue Eagles, Sulom inasintha masewero a Bullets a Loweluka kuwaika Lachisanu ndi cholinga choti osewera onse a timuyi kuphatikiza omwe ali ndi Flames asewere nawo masewero-wa.
Malingana ndi timu ya apolisi-yi, ngakhale kuti osewera awo atatu (Schumacher Kuwali, Micium Mhone komanso Sankhani Mkandawire) ali ndi timu ya Malawi, akuwapasa masewero sabata ya mawa.
Iwo ati ndi zodandaulitsa kaamba koti osewera awo ena kukhala kulibe pa masewero awo ndi TN Stars.
Aka ndi kachiwiri timu ya Blue Eagles kudandaula ndi momwe Sulom ikuikira masewero ake amu ligi ya TNM.
Bwanji ma predictions anga akuchepa m'malo mwa 27 ikuwonesa 8 predictions zikukhala bwanj admin
Oky boss ndakumvani
Timawerenga ma prediction olondola mu chaka chimodzi (ma week 52 omwe adutsa).
Bullets Palibe atawaimitse apa. Mateam akapanga chibwana akhoza kumaliza season yose osachinyidwa
Bwaji za nbb reserve
Kodi manoma ali ndizigoli zingati?
Manoma agoletsa zigoli 21 mu Super League.
Go igwina go we need draw or win tomorrow karonga fc Moto unandi
Timu ya Nyasa Big Bullets masanawa ikumana ndi Sable Farming pa bwalo la Kamuzu mu mzinda wa Blantyre.
Mphunzitsi wa Bullets, Kalisto Pasuwa, wati timu yake ndi yakonzeka kuchita bwino pa masewero.
A Pasuwa ali ndi chikhulupiliro kuti osewera ake alimbikira kuti atenge mapoint onse atatu.
Padakali pano, Bullets ili pa nambala 1 ndi mapoint 38 pa masewero 14 omwe yasewera pamene Sable Farming ili ndi mapoint 11 pa masewero 13 omwe yasewera ndipo ili pa number 14.
MPILA PAKATI PA BB NDI SEBLE FAMING
Mpila Ndani ku wina
NBB Will Win By 4-0
Tieni tipatsemoto timuyathu ya noma pa 2 pakubwelapa
[image]
π²πΌπ²πΌ
#TNMSuperLeague
Andrew wawina mphoto ya K5,000πΈ atalosera molondolaπ― magemu 3 kuposa ena onse sabata yatha pa owinna.comβ½
Kuyambira July sabata yamawa, olosera molondola magemu ambiri kuposa ena onse adziwina kapena kugawana mphoto ya K10,000! πΈ