Login with Facebook to post predictions, updates & live scores
Chelsea vs Liverpool
Chelsea vs l
MALAWIANS OUTSIDE MALAWI
â. Chawanangwa Kaonga played 79 minutes of the game as Zanaco drew 0-0 with NAPSA Stars in Zambia
â. Robert Saizi played his second match as a substitute after given the last 35 minutes as Zanaco drew 0-0 against NAPSA.
â. Chifundo Mphasi played for 93 minutes as Kabwe Warriors played a goalless draw against Prison Leopards in the Kabwe Derby.
â. Gabadinho Mhango was a starter as Moroka Swallows beat Platinum City Rovers 3-1 on penalties after a goalless draw in 120 minutes.
â. Khuda Muyaba played for 73 minutes as Richards Bay beat Polokwane City 3-2 in the Ned Bank Cup. It was his debut.
â. Shaquille Gwengwe played the match which Dorchester City drew 2-2 with Heton.
â. Yamikani Chester scored a goal as Costa do Sol lost 1-2 to Ferroviario de Maputo in the first leg of the Jogibelt League.
â. Richard Mbulu, Lloyd Njaliwa and Chikoti Chirwa also played the match.
"CHITIPA IWONJEZANO MOTO" - KAFOTEKA
Wachiwiri wa mphunzitsi wamkulu ku Chitipa United, Elvis Kafoteka, wati ndikhumbo lake kuti anthu onse kutimuyi agwirire ntchito limodzi ndi cholinga choti adutse pomwe anafikira chaka chatha.
Kafoteka wayankhula patsogolo pa ligi ya chaka chino ndipo walonjeza kunena kuti ayesetsa kuthandiza timuyi kuti ifikire ku mtunda kwa matimu atatu oyambilira mu ligi.
"Ndingopempha kuti tonse tigwirane manja kuti zikatero tikhonza kudutsa pomwe tinafika chaka chatha ndipo tikhonza kukakhazikika kumtunda kwenikweni kwa ligiyi. Chaka chino kuli moto wochuluka ku Chitipa." Anatero Kafoteka.
Iye agwira ndi a McNerbert Kadzuwa ngati mphunzitsi wamkulu pomwe a Gift Mkamanga ndi wachiwiri wake. Timuyi Inathera pa nambala yachinayi mu ligi ya chaka chatha.
REPORTS: WANDERERS FORGAVE BUTAO
Mighty Mukuru Wanderers are ready to welcome back Mike Butao at the club to replace the out going acting Chief Executive officer, Roosevelt Mpinganjira, in 2024 season.
A source from inside has confirmed to us that Butao has been a long mentioned name to be part of the team as they look to restore the lost glory. After asked about the money laundering charges on him, we were told he is free.
"Butao has been a favorite to come back, Mpinganjira has just left a void for him to fill. About the money laundering charges, he was forgiven by the team." Said the Source.
Butao was part of the team that won the league in 2017 and the team has also called back Steve Madeira to be part of the team.
The team has parted ways with Mpinganjira today, eight months after working with the Nomads.
WANDERERS YACHOTSA MPINGANJIRA
Timu ya Mighty Mukuru Wanderers yachotsa ntchito mkulu watimuyi (CEO), a Roosevelt Mpinganjira kuyambira loweruka masana.
A Mpinganjira atsimikiza okha za kuchotsedwaku koma sanafotokoze zambiri pankhaniyi.
Ena mwa akuluakulu atimuyi sanalinso opezeka kuti ayankhulepo pa nkhaniyi.
Mpinganjira wakhala kutimuyi kwa miyezi isanu ndi itatu yokha chimulembereni ndipo anali yekha wotsalapo pomwe Manoma anathetsa komiti yawo yonse mwezi watha.
This is the official UEFA Europa League round of 16 draw that has been conducted on Friday by UEFA:
đ¨đż Sparta Prague - Liverpool đ´ó §ó ˘ó Ľó Žó §ó ż đŚđż Qarabag - Leverkusen đŠđŞ đŽđš Roma - Brighton đ´ó §ó ˘ó Ľó Žó §ó ż đŽđš Milan - Slavia Prague đ¨đż đŠđŞ Freiburg - West Ham đ´ó §ó ˘ó Ľó Žó §ó ż đŤđˇ Marseille - Villarreal đŞđ¸ đľđš Benfica - Rangers đ´ó §ó ˘ó łó Łó ´ó ż đľđš Sporting - Atalanta đŽđš
NEWS
FCB Nyasa Big Bullets has today presented the first kit to club legends ahead of the Blantyre derby against Mighty Mukuru Wanderers FC legends at Kamuzu Stadium on 4 March.
The two teams will face in a bid to find funds for their Association that will look at the welfare of the legends of both teams.
.NKHANI
Timu ya FCB Nyasa Big Bullets ikhonza kusaina osewera yemwe wangochotsedwa ku Wanderers posachedwa, Matthews Masamba.
Osewerayu akuti wakondweretsa aphunzitsi atimuyi pomwe akuyesa mwayi ndipo atha kutsala kutimuyi.
Masamba anagulidwa ndi Wanderers mu 2022 kuchokera ku Bangwe All Stars ndipo amasewera pakati. Iye anapititsidwa pangongole mchigawo chachiwiri cha ligi ya chaka chatha ku Bangwe konku koma tsopano chaka chino amuchotsa.
From Kondowe to Masamba
MPONDA INCLUDE ZICCO MKANDA IN SILVER'S PANEL
Silver Strikers head coach has announce the inclusion of his former Striker at FCB Nyasa Big Bullets, Zicco Mkanda, to be the team's strikers in the coming 2024 season.
Mjojo said this on Friday as he unceiled his backroom staff for the coming season and believes Mkanda will help him a lot.
"The reason for bringing Mkanda, he has been one of the finest strikers in this years and with his experience he will help the youngsters, I think the players also have seen him playing so they will learn from him." Said Mponda.
Here is how the whole technical panel appears:
Head coach: Peter Mponda First deputy: Peter Mgangira Second deputy: Young Chimodzi Jr Strikers trainer: Zicco Mkanda Goalkeepers trainer: Victor Mphande Team manager: Emmanuel Chipatala Welfare manager: Cassim Wasiri Team doctor: Chikondi Kaminga Physiotherapist: Andrew Ntalimanja Data analyst: Taonga Chimodzi
Reported by Hastings Wadza Kasonga Jr
RAMADAN ABWERA MWEZI WA MAWA
Mphunzitsi watimu ya Mighty Mukuru Wanderers, Nsanzurwimo Ramadan, sanafikebe kutimuyi ndipo akuyembekezeka kudzayamba ntchito pa 1 March 2024.
Mkulu woyendetsa ntchito zatimuyi, Tiyasomba Banda, watsimikiza zankhaniyi kunena kuti mphunzitsiyu akadali ndi timu yomwe akuphunzitsabe ku Tanzania koma achoka kumapeto a mwezi uno.
"Mphunzitsiyu anapereka kalata kuti achoka kumapeto amwezi uno komwe akugwirako nde tikumuyembekezera kuti afika pa 1 March. Sitikudandaula chifukwa ndi zimenenso tinkayembekezera nthawi yomwe tinkamupatsa ntchito." Anatero Banda.
Padakali pano, wachiwiri kwa mphunzitsiyu, Meke Mwase ndi amene akutsogolera timuyi.
Mphunzitsiyu anauzidwa kuti ayitsogolerere timuyi kutenga ligi ya TNM komanso zikho ziwiri zapadera ndipo chimodzicho atha kusiyirako ena.
CRECK YATOLA KAMWENDO
Timu ya Creck Sporting Club yalengeza kuti yatenga Joseph Kamwendo kuti akhale wachiwiri kwa mphunzitsi.
Iye watsimikiza za nkhaniyi ndipo athandizira Macdonald Mtetemera yemwe ndi mphunzitsi.
"I CANT COACH LOCAL CLUBS" - KINNAH
Former Flames coach, Kinnah Phiri, says he can return to coaching now after the change of leadership at Football Association of Malawi but can only go for national team and foreign clubs.
Phiri said he announced that he will never coach in Malawi after his disrespectful dismissal as a Flames coach in 2012 but he has now left the decision but now wants big things only.
"I said will not coach in Malawi again but now I withdrew those words because if the changes at FAM, I am open to coach but only at National team not local clubs because the job I'm having now is huge, only if they want mentorship I am open." Said Phiri.
The coach is currently working as a deputy director of sports at the ministry of Sports. He was the second ever Coach to take Malawi to the African Cup of Nations in 2010.
CHITIPA YATENGA KADZUWA
Timuya Chitipa United tsopano yalemba mphunzitsi wamkulu, McNorbert Kadzuwa, kuti atsogolere timuyi mu chaka cha 2024.
Iye akhala akuthandizidwa ndi Elvis Kafoteka komansotu Gift Mkamanga.
Iye walowa mmalo mwa Macdonald Mtetemera yemwe wapita ku Creck Sporting Club.
LWEMBA TO WANDERERS IS A FAILED DEAL
Mighty Mukuru Wanderers might fail to sign one of their targets this summer, Chitipa United's defender, Chris Lwemba as an insider has labelled it as they are 'not serious.'
The insider told us that the Nomads offered Lwemba a contract of a huge period but little money and a little salary of which the player is not interested as he believes he is a 'big player.'
Meanwhile, Chitipa United's officials have advised the captain not to move to the Nomads as the money being offered can not take him anywhere because its just very little.
The source further said the player is said not shaken by a move away from Chitipa and that he will play until his contract ends in December this year.
CHITIPA YATENGA KAFOTEKA
Timu ya Chitipa United yalengeza kuti yatenga mphunzitsi watimu ya Extreme FC, Elvis Kafoteka kuti awatsogolere mu ligi ya chaka chino.
Kafoteka wasaina mgwirizano wa zaka ziwiri ndi timuyi ndipo polemba pa tsamba lake la Facebook wathokoza anthu onse ku Extreme FC kamba kokhala naye bwino.
Iye wati akuyembekezera zabwino kutimu ya Chitipa kuti ikhalanso ikuchita bwino mu ligi.
Iye walowa mmalo mwa Macdonald Mtetemera yemwe anachoka kutimuyi chaka chatha kupita ku Creck Sporting Club.
"NDIKUFUNA NDITAVALA MENDULO CHAKA CHOYAMBA" - KUDONTO
Wosewera yemwe wakwezedwa kupita kutimu yaikulu ku Mighty Mukuru Wanderers, Dan Kudonto, wati alibe mantha kutumikira timuyi ndipo akufunitsitsa atavala mendulo mu chaka chake choyamba.
Iye wati umoyo wake kutimuyi wayamba bwino ndipo akiyembekezera kaye kuphunzira zambiri kuchokera kwa ankhala kale kutimuyi komabe akukhulupilira kuti Wanderers situluka chimanjamanja chaka chino.
"2024 ndayikonzekera bwino kwambiri ndipo zinthu ndipanga. Mukudziwa kuti ikhala season yanga yoyamba kumenya supa ligi ndiye kuzikhalabe kuphunzira koma ikhala season yabwino matimu aatiziwa."
Kudonto amasewera pakati motchinga ndipo ndi mmodzi mwa osewera omwe akwezedwa kuchokera kutimu yachisodzera yomwe inakwanitsa kutenga zikho ziwiri chaka chatha.
Wolemba Hastings Wadza Kasonga Jr
BANDA SCORES AS UD SONDO BEAT SUPERSPORT
Flames captain, Christopher John Banda, scored the fourth goal of UD Songo as they beat Supersport United 2-4 in a friendly on Thursday morning.
This is their second pre-season friendly in South Africa after they drew 1-1 with Polokwane City on Monday.
Miracle Gabeya was not a starter in this match same as Banda, who came off the bench to score the final goal.
Akunja mumamvera pano!
SIGNED
Mighty Mukuru Wanderers has completed the signing of left back, Timothy Silwimba.
The defender has penned a three year deal with the Nomads and will be unveiled at the Blue camp next week.
Next is Lwemba.
SILWIMBA TO WANDERERS
Civo United captain and left back, Timothy Silwimba, has left the team as he is on verge of joining Mighty Mukuru Wanderers ahead of the upcoming season.
Reports suggests that the defender has already said goodbye to his teammates and that any day, he will be announced by the Nomads.
The team has been in search of a left back after using Isaac Kaliati and Wisdom Mpinganjira on the position.
Meanwhile, the team is also set to announce the signing of Chris Lwemba any day next week.
PLAYERS AWARDS
BEST GOALKEEPER Richard Chimbamba - FCB Nyasa Big Bullets
DISCOVERY OF THE TOURNAMENT Emmanuel Savieli - Bangwe All Stars
GOLDEN BOOT . 1. Peter Kasonga 2. Mphatso Philimon 3. Emmanuel Saviel 4. Chiukepo Msowoya 5. Gastin Sinkonda 6. Patrick Macheso
PLAYER OF THE TOURNAMENT: Lanjesi Nkhoma - FCB Nyasa Big Bullets
2023 CASTEL CHALLENGE CUP MEDIA AWARDS
BEST PRINT JOURNALIST Isaac Salima (Times Group)
BEST TV JOURNALIST Hankey Chimtengo (Mibawa TV)
BEST ONLINE JOURNALIST Joseph Dumbula (MIJ Online)
BEST RADIO REPORTER Richard Tiyesi (Timveni Radio)
BEST PHOTOJOURNALIST Bobby Kabango (Nation Publications Limited)
BEST COMMUNITY RADIO JOURNALIST-NORTHERN REGION Victor Musongole (Tingabane Radio)
BEST COMMUNITY RADIO JOURNALIST-CENTRAL REGION Jameson Kalimba (Ntunthama Radio)
BEST COMMUNITY RADIO JOURNALIST-SOUTHERN REGION George Sulumba (Ndirande FM)
CASTEL YALEDZERETSA MPIRA KU MALAWI
Kampani yofulula mowa ya Castel Malawi ichititsa kuti anthu aledzere tsopano ndi masewero a mpira pomwe yaonjezera ndalama zomwe imapereka ku chikho Cha Castel ndi ndalama zokwana K80 million mu chaka cha 2024.
Mkulu woyendetsa kampaniyi, a Thomas Reynaud, ndi omwe atsimikiza zankhaniyi ku hotelo ya Amaryllis mu mzinda wa Blantyre pa mwambo wopereka mphoto kwa omwe anachita bwino chaka chatha.
Iwo ati ndalama zomwe anayika chaka chatha zokwana K320 million tsopano zifika pa K400 million ndipo opambana azilandira K55 million kuchoka pa K50 million.
Poyankhulapo, mtsogoleri wa Football Association of Malawi, Fleetwood Haiya, anathokoza kampaniyi ndipo wati chifukwa cha kuzipereka kwawo, bungwe liwathandiza kugulitsa malonda awo kudzeranso mu mpikisanowu.
Mu chaka choyamba, FCB Nyasa Big Bullets ndiyo inapambana chikhochi itagonjetsa Silver Strikers 4-2 pa mapenate.
Wolemba: Hastings Wadza Kasonga Jr
A NKUNIKA ATSOGOLERABE MASAPOTA A WANDERERS
Timu ya Mighty Mukuru Wanderers yatulutsa mayina a ochemerera atimuyi omwe akhale akutsogolera anzawo kwa zaka ziwiri zikubwerazi.
Mu kalata yomwe wasaina mmodzi mwa akuluakulu a board ya timuyi, Chancy Gondwe, yotulutsidwa lachinayi yati a Mervin Nkunika ndi omwe atsogolerebe ochemererawa ndipo a Bishop Chimwenje akhala owatsatira ndipo mlembi wamkulu ndi Davie Pemba komanso Chikhulupiliro Mphatso awatsatira.
Timuyi yaikanso chigawo chakummawa ngati gawo lina kuphatikiza pa kumpoto, pakati komanso kummwera.
A Mike Kamanga atsogolera chigawo chapakati, a Joseph Bolamoyo atsogolera kumpoto, a Dennis Chitsulo kummwera ndiponso a Davie Monjeza atsogolera kummawa.
"SILVER INALI TIMU YAKUMALOTO KWANGA" - CHIKOOKA
Goloboyi yemwe timu ya Silver Strikers yangosaina kumene, George Chikooka, wati linali khumbo lake kudzasewerako timu ngati Silver Strikers ndikuti agwira ntchito molimbikira.
Iye amayankhula atasaina mgwirizano wake wa zaka zitatu ndi timuyi kutsatira kuchoka kutimu ya Chitipa ndipo wati palibenso chilendo chilichonse chomwe ataone ku Silver Strikers.
"Ndine wokondwa pobwera kutimuyi, anali maloto anga ntadzasewerako kutimuyi ndipo ndingoyamika Mulungu pokwanilitsa malotowa. Palibenso chilendo chilichonse chomwe ndingaone, enawa takhala tikusewera nawo nde palibe chilendo." Anatero Chikooka.
Katswiriyu anali mmodzi mwa magoloboyi omwe anachita bwino mu ligi ya chaka chatha pomwe sanagoletsetse mmasewero 12 ndipo alimbirana pa malo oyamba pagolo ndi Charles Thom komanso Pilirani Mapira.
"MASAPOTA AYEMEKEZERE ZAMBIRI ZOKOMA" - KATINJI
Katswiri yemwe wasainidwa nditimu ya Silver Strikers, Binwell Katinji, wati ochemerera atimuyi ayembekezere zabwino zokhazokha pomwe wati agwira ntchito ngatinso mmene amachitira kumatimu ena.
Iye amayankhula atasaina mgwirizano wa zaka ziwiri kutimuyi kutsimikiza za kubwereranso kutimuyi ndipo wati ndi wokondwa kubwereranso kwawo.
"Ndine wosangalala poti ndabwereranso ku Silver, nditimu yoti ndasewerapo, khalidwe lake ndikulizidziwa komanso zambiri nde ndasangalala. Masapota amayembekezera zambiri koma ndi zoti sindingagwire ntchito ndekha komabe ayembekezere zabwino zambiri ngati mmene ndimachitira ku matimu ena." Anatero Katinji.
Katswiriyu wapita kutimuyi mwaulere kutsatira kutha kwa mgwirizano wake ndi Civo komwe anamwetsa zigoli 12 mu ligi ya chaka chatha.
TWO BULLETS NOMINATED FOR PLAYER OF THE SEASON AWARD
Airtel Top 8 Champions, FCB Nyasa Big Bullets, has its two strikers, Lanjesi Nkhoma and Maxwell Gasten Phodo been nominated for the player of the tournament alongside Christopher Mikuwa of MAFCO.
This has been disclosed by the Football Association of Malawi on Wednesday saying different coaches were the ones who did the nominations.
Meanwhile, Lanjesi Nkhoma was the golden boot winner with three goals, of which two won the cup in the final.
FCB Nyasa Big Bullets had to beat MAFCO 2-1 in the final to win the tournament for the second time.
FC Bayern Munich have announced that they will part ways with head coach Thomas Tuchel in the summer.
ATSIGAH WAPITA KU BANGWE
Timu ya Bangwe All Stars ikupitiliza kuzilimbitsa patsogolo pa ligi ya chaka cha 2024 pomwe yatenga katswiri watimu ya Karonga United, Eric Atsigah, kuti atumikire timuyi.
Atsigah, yemwe kwawo ndiku Ghana, watsanzika ku Karonga pomwe wakana kuonjezera mgwirizano wake ndi timuyi ndipo tsopano wati akubwereranso mu mzinda wa Blantyre.
Iye wasewerapo matimu a Masters Security ndi Mighty Mukuru Wanderers asanapite ku Karonga.
Timu ya Bangwe sinatsimikize za osewerayu pomwe zikumvekanso kuti yasaina ena monga Davie Tobias, Ghedo Lorenzo, Rajab Nyirenda, Josiah Duwa komanso Justice Honde.