.NKHANI
Timu ya FCB Nyasa Big Bullets ikhonza kusaina osewera yemwe wangochotsedwa ku Wanderers posachedwa, Matthews Masamba.
Osewerayu akuti wakondweretsa aphunzitsi atimuyi pomwe akuyesa mwayi ndipo atha kutsala kutimuyi.
Masamba anagulidwa ndi Wanderers mu 2022 kuchokera ku Bangwe All Stars ndipo amasewera pakati. Iye anapititsidwa pangongole mchigawo chachiwiri cha ligi ya chaka chatha ku Bangwe konku koma tsopano chaka chino amuchotsa.
From Kondowe to Masamba
Login with Facebook to post predictions, updates & live scores