CHITIPA YATENGA KADZUWA
Timuya Chitipa United tsopano yalemba mphunzitsi wamkulu, McNorbert Kadzuwa, kuti atsogolere timuyi mu chaka cha 2024.
Iye akhala akuthandizidwa ndi Elvis Kafoteka komansotu Gift Mkamanga.
Iye walowa mmalo mwa Macdonald Mtetemera yemwe wapita ku Creck Sporting Club.
Login with Facebook to post predictions, updates & live scores