Patrick Mabedi komanso Declerk Msakakuona sanasainebe kontrakiti kuti akhale aphunzitsi a matimu a chisodzera a dziko lino.
Aphunzitsi-wa anakhoza mayeso omwe FAM inali nawo okhudza ntchitozi.
Login with Facebook to post predictions, updates & live scores