Malawi elite FIFA Assistant Referee, Bernadettar Kwimbira, will this evening make history when she joins the first ever all women refereeing team to officiate a match at the ongoing CHAN competition.
In the on going football season, Mighty Wanderers is yet to win a game at its home ground, Kamuzu Stadium.
The team has also failed to score a goal at the stadium.
Timu ya Ntopwa ili mavuto azachuma ndipo ikulephera kulipira kukwanilitsa zinthu zina kaamba kosowa ndalama.
Mkulu oyendetsa ntchito za timuyi, Isaac Jomo Osman, ndiye wanena izi.
Gabadinho Mhango akhala osasewera masewero ali onse kwa sabata ziwiri zikudza kaamba kovulala.
Malingana ndi madotolo a timu ya Orlando Pirates, katswiri omwetsa zigoliyu anavulala Lachitatu.
Timu ya Flames isewera ndi South Sudan mu mpikisano ofuna kuzigulira malo ku AFCON m'mwezi wa March.
Masewerowa azachitika pa 24 March ndipo pa 29 mwezi omwewu asewera masewero omaliza ndi Uganda.
Sheriff Tiraspol of Moldova have commenced preparations for the new season.
The team has invited new players for trials ahead of the season.
Flames and Nyasa Big Bullets player, Peter Banda, is among the players to undergo trials.
Live 0-1 (Barnes 83' [P])
81' 0-0
60' 0-0
46' 0-0
HT 0-0
36' 0-0
17' 0-0
2' 0-0
Mtsogoleri wa bungwe loyendetsa masewero a mpira wa miyendo mdziko muno la FAM, Walter Nyamilandu, walimbikitsa anthu okhudzidwa ndi masewerowa kutsatira njira zopewera matenda a COVID-19.
Mtsogoleri wa FAMyu wati kuimitsidwa kwa masewero kwa sabata zitatu kusabwenze anthuwa mbuyo potsatira ndondomekozi.
Iwo ati posachedwapa anthu akhala akuonera masewero a mpira.
Woyang'anira oyimbira ku bungwe la CAF wayamikira woimbira waku Malawi, Bennerdetter Kwimbira, pammene anagwirira ntchito yake pa masewero amu mpikisano wa CHAN Lachiwiri.
Prediction 2-0 prediction
Manchester United have completed their first round Premier League matches with a 1-2 win over Fulham.
The team is on position 1 and 2 points clear over rivals, Manchester City who are on position 2.
Manchester United are back on top of the Premier League following a 1-2 win over Fulham.
81' 1-2 (A. Lookman 5' - E. Cavani 21', P. Pogba 65')
Live 1-2 (A. Lookman 5' - E. Cavani 21', P. Pogba 65')
Live 1-2 (A. Lookman 5' - E. Cavani 5', P. Pogba 65')
61' 1-1 (A. Lookman 5' - E. Cavani 21')
HT 1-1 (A. Lookman 5' - E. Cavani 21')
30' 1-1 (A. Lookman 5' - E. Cavani 21')
Live 1-0 (Lookman 5')
Gerald Phiri Jnr scored a goal to help his club, Baroka collect 3 points against Stellenbosch.
Phiri scored the third goal for his club.
Live 2-0 (B. Silva 79', Gundogan [P])
Live 1-0 (B. Silva 79')