Timu ya BE FORWARD Wanderers yati yasiya zokambirana ndi Blue Eagles pomwe amafuna kugula wosewera wa timuyi, Vitumbiko Kumwenda.
Mlembi wa Wanderers, Victor Maunde, watsimikiza za nkhaniyi.
Login with Facebook to post predictions, updates & live scores