Login with Facebook to post predictions, updates & live scores
Silver 1 - 0 Kamuzu Barracks
mozambiqu moto kuti buu
KOMITI YAVOMEREZA MAYINA A PACHISANKHO CHA FAM
Komiti yaikulu yomwe ikuyang'ana za chisankho cha bungwe la Football Association of Malawi lavomereza mayina a anthu omwe anasankhidwa ndi mabungwe omwe amavota kuti akayimire pa chisankhochi.
Komitiyi imakumana loweruka kuti iunikire mayinawa ndipo yavomereza mayina awa:
PRESIDENT 1. Fleetwood Haiya 2. Walter Nyamilandu Manda
FIRST VICE PRESIDENT 1. Christopher Madalitso Kuyera 2. James Mwenda
SECOND VICE PRESIDENT 1. Dr Lameck Khonje 2. Othaniel Hara
EXECUTIVE MEMBERS 1. Daudi Ntanthiko 2. Chancy Gondwe 3. Patrick Kapanga 4. Bernard Harawa 5. Raphael Humba 6. Chimango Munthali 7. Muhammad Selemani
WOMENS REPRESENTATIVE 1. Felister Dossi 2. Mervis Mangulenje
Mu kalata yosainidwa ndi wapampando wa komitiyi, yapereka mphamvu kwa anthu omwe ali ndi vuto ndi mayinawa. Kuti akhonza kukaneneza kuti achotsedwe pa ndandandawu.
CHAWINGA'S PSG WIN IN FRANCE
Scorchers forward, Tabitha Chawinga, played the match as PSG Women depended a last minute winner to beat FC Fleury 91 2-1 in the D1 Arkema in France on Sunday afternoon.
The Parisans led through Katoto on 13th minutes but the visitors levelled through Kamczyk on 39th minute to go to break tied at 1-1.
In the second half, it was tight for the hosts as PSG tried their level best to find a winner of which they were denied several times but Jackie Groenen pounced in on the 96th minute to seal the winner.
"ONE OF THEIR PLAYERS WERE OFFSIDE" - CHIRWA
Dedza Dynamos head coach, Gilbert Chirwa, says the referee could have denied the Ekwendeni Hammers' equaliser in their match as one of the players was offside.
Chirwa said this after the match which his team lost 6-5 on penalties after a 1-1 draw in the regulation time and blamed the officiation for awarding the goal but says they will switch attention to their next game against FCB Nyasa Big Bullets.
"The game was good and we were leading 1+0 and Ekwendeni equalised through a free kick but I think one of their players was completely offside and the whole bench was surprised as to why they did not raise the flag otherwise penalties are unpredictable, they won." Said Chirwa.
Christopher Phiri netted an opener on 16th minute via a penalty but Chisomo Sambani's header on 65th minute forced the game into the penalty where Charles Chipala's miss gifted Hammers a win.
The team turns attention to the league where they will play FCB Nyasa Big
Ndikufunila zabwino zonse timu ya maliwi pamene ikukumana ndi tunizia malawi 2 inayo 0
2-2
WANDERERS YAUMITSABE MTIMA
Timu ya Mighty Mukuru Wanderers yati ikasumanso kachiwiri pa chiganizo cha timuyi kamba koti bungwe la Football Association of Malawi silinachite kalikonse pa dandaulo lawo la poyamba.
Timuyi inasuma itapatsidwa chilango kuti ilipire K24.5 million komanso kuti inagonja 2-0 ndi Silver Strikers mmasewero awo a Airtel Top 8 koma bungweli silinasinthepo kalikonse.
Mmodzi mwa akuluakulu atimuyi, Chancy Gondwe, wati timuyi yachita chiganizo chokasumanso.
"Tikati tiunikire pa chigamulo choyamba chija ndi ichi palibe chimene chasinthapo nde ifeyo zomwe tinanena sizinamveke." Anafotokoza Gondwe.
Timuyi imayenera kusewera ndi Silver Strikers mu masewero achibwerenza loweruka sabata ya mawa pa 25 November koma zateremu mpikisanowu uchedwa kaye poti atha kulepherekanso.
Source: wa mpira
"NDAKONDWA POTI TAPAMBANA KOYAMBA KU WEST AFRICA" - MABEDI
Mphunzitsi watimu ya Flames, Patrick Mabedi, wati ndi wosangalala ndi chipambano cha timu yake ndipo wayamikira osewera kamba kosewera ndi mmene anawauzira kuti mpaka agonjetse Liberia 1-0.
Mabedi amayankhula atatha masewerowa ndipo wati zovuta zinalipo zambiri mmasewerowa komabe anyamata anayesetsa mpaka aphwanya mbiri yosapambana ku maiko akumadzulo kwa Africa.
"Mmene timabwera kuno tinapanga plan molingana ndi nyengo yakuno kuti ndi yotentha kwambiri. Mchigawo choyamba anyamata amachitako timantha pomwe samapatsirana koma titawayankhula zinasintha. Mchigawo chachiwiri kunali mvula komabe tinawauza kuti asasunge mpira kumbuyo poti umatha kuima nde liwiro la osewera latithandiza kuti tipambane." Anatero Mabedi.
Timuyi ikumana ndi Tunisia lachiwiri likudzali pa bwalo la Bingu pa masewero enanso amu gulu H lomwe Malawi tsopano ili pa nambala yachitatu pa matimu asanu ndi imodzi.
Wolemba: Hastings Wadza Kasonga Jr
CHITIPA UNITED YAPAMBANA MPHOTO KU MPOTO AWARDS
Timu ya Chitipa United yasankhidwa kukhala timu yapamwamba mu chaka cha 2023 itagonjetsa matimu ena anayi mmavoti kamba koti inapeza ochuluka kwambiri kuposa enawo.
Chitipa inagonjetsa timu ya Karonga United ndi Ekwendeni Hammers, onse amu Supa ligi komanso ena awiri amu Basketball a Nkhande komanso Pistons akumpoto komweko.
Kumbali ya wosewera wapamwamba kuposa onse ku matimu akumpotowa, Priscilla Soko wa Chimwavi Smashers ndi yemwe wapamwamba atagonjetsa Macdonald Harawa ndi Gastin Simkonda a Moyale Barracks komanso Jimmy Msiska wa Ekwendeni Hammers.
Aka kanali koyamba kuti a mpoto awards apereke mphoto kumbali ya zamasewero ndipo mphotozi zimapita kwa anthu okha okha ndi matimu akumpoto kwa dziko lino.
amalawi tamwela wakaka
WELODI CAP AMALAWIFE TILOWANAWO TANGOLIMBIKILA BAS
🚨🚨BREAKING: Everton have received a 10-point deduction, which will be applied immediately, after being found to have breached the Premier League's financial fair play rules.
They have now dropped from 14th to 19th on the Premier Legue table.
NYONDO AND CHIPALA FIT FOR GAMES AT DEDZA DYNAMOS
Dedza Dynamos has received a major boost in their upcoming matches after their two prolific forwards, Clement Nyondo and Charles Chipala, return to the pitch as they have recovered from their injuries.
The team will play the Castel Challenge Cup round of 16 match against Ekwendeni Hammers on Sunday before winding up their two TNM Super league fixtures and coach, Gilbert Chirwa believes his team could finish strong with the recent developments.
"We were hit hard by injuries to our strikers and their return is a big boost to the team ahead of our final games this season," Chirwa said to the team's media crew.
He further said the team's current performance isn't that pleasing but they will try to finish the season on high.
"We understand the frustrations from our fans and they should understand that no one is happy with our performance including us and the players but every challenge comes up with a success story," Chirwa explained.
PALIBE CHOSINTHA PA CHILANGO CHA WANDERERS
Timu ya Mighty Mukuru Wanderers tsopano ikuyenera kukumana ndi timu ya Silver Strikers mmasewero achibwerenza a chikho cha Airtel Top 8 akugonja 2-0 pomwe bungwe la Football Association of Malawi sinasinthebe pa chigamulo chawo.
Bungweli latulutsa chigamulochi lachitatu madzulo pomwe dandaulo la Manoma silinamveke ndipo ikonzabe mipando yapa bwalo la Bingu komanso kulipira ndalama za nkhaninkhani.
Zina mwa zinthu zomwe zili mu chigamulochi ndi izi:
1. Masewero adathera 2-0 kukomera timu ya Silver Strikers ndipo achibwerenza aseweredwa pa 25 November 2023.
2. Manoma awuzidwa kuti alipire ndalama zokwana K500,000.00
3. Timu ya Mighty Mukuru Wanderers ikonzetse chirichonse chomwe ochemelera awo adaononga pabwalo la Bingu pomwe matimu awiriwa amakumana.
4.Timu ya Nyerere ilipire K2 million kamba kolephera kuletsa ochemelera awo pa mchitidwe omwe adaonetsa patsikuli potengera kuti ananyazitsa masewerowa.
Timu ya Wanderers ili ndi mwayi woka
1~0
TABITHA, TEMWA AND FAZILI NOMINATED FOR CAF AWARDS
Malawi's blessed and talented sisters, Tabitha and Temwa Chawinga, have been nominated for the CAF Women's Footballer of the year award by the Confederations of African Football following impressive outings in 2023.
Tabitha became the first African female footballer to win a golden boot in Italy after netting 23 goals in Serie A Feminine and won the Chinese Womens Super Cup with Wuhan Jiangda after her loan deal expiring with Inter.
Meanwhile, her sister, Temwa, helped Scorchers to win their first ever COSAFA Women's Championship in South Africa and has won two golden boots awards in China with Wuhan Jiangda and looking for her third as she leads with 24 goals in Chinese Women's Super League.
The Scorchers have been nominated as the best Women's Football team of the year while their coach, Lovemore Fazili has been nominated as the Women's Football coach of the year.
The 2023 CAF Awards Gala will be held on December 11 in Marrakech
MPHUNZITSI WAYIMITSIDWA KAMBA KOSOWA KHALIDWE
Timu ya Ekwendeni Hammers yaimitsa wachiwiri kwa mphunzitsi wawo, Luckson Mauluka Nyoni, kamba ka zifukwa zosowa mwambo malingana ndi timuyi.
Timuyi yati mphunzitsiyu anachita zinthu zomwe sizinakomere timuyi pa masewero omwe anagonjetsa Civo United 3-2 pa bwalo la Rumphi sabata yatha ndipo mpake amuyimitsa.
Koma poyankhapo, Nyoni wati sakudziwa za nkhaniyi poti sanalandire kalata iliyonse komanso kuti anatsanzika pamasewero omwe timuyi inagonja 3-1 ndi Silver Strikers basi.
Mauluka ndi mmodzi mwa aphunzitsi omwe akhalitsako kutimuyi kuchokera mu chaka chomwe inalowa mu ligi ndipo timuyi ikumenyera nkhondo yoti isatuluke mu ligiyi.
Source: Wa Mpira
NTAFU WASEWERA BWINO KU CHITIPA MU OCTOBER
Katswiri wa Chitipa United, Ramadhan Ntafu, wasankhidwa kukhala wosewera wapamwamba kuposa onse mu mwezi wa October atalandira mavoti ambiri kutimuyi.
Ntafu wagonjetsa Jack Beza komanso Godfrey Kwiyokwa pamavoti omwe ochemerera atimuyi amasankha kudzera pa tsamba lawo la mchezo ndipo iye atenga ndalama zokwana K100,000 kuchokera ku Green Villages.
Tabitha Chawinga is in the D1 Arkema week 7 team of the week in France after netting a hat trick for PSG.
This is the second time to appear in this chart.
GABA WATSALA KU LIBERIA
Timu ya Flames sikhala ndi katswiri wawo wa kutsogolo, Gabadinho Mhango, mmasewero omwe akumane ndi timu ya Liberia mu masewero opitira ku World Cup kamba koti ndege yopita ku Ethiopia yamuthawa.
Katswiriyu amayenera kunyamuka mdziko la South Africa lamulungu kuti akakumane ndi timu yonse ku Ethiopia pa ulendo wawo opita ku Liberia koma wasemphana nayo ndegeyi.
Timuyi sikhalanso ndi katswiri wa Pakati ku FCB Nyasa Big Bullets, Frank Willard, yemwe wavulala mmasewero omwe timu yake inalepherana 0-0 ndi Blue Eagles.
Osewera atatu, Christopher Kumwembe, Olson Kanjira komanso Mhango ndi omwe anatengedwa kuti akasewere kutsogolo kwa timuyi ndipo Chifundo Mphasi ndi Lanjesi Nkhoma ndi ena omwe atha kulowa mmalo mwa katswiriyu.
MKANDAWIRE WAKAYA MOTO KU ZAMBIA
Katswiri waku Malawi wosewera mpira wamiyendo koma ali mzimayi, Mercy Vitumbiko Mkandawire, wayaka moto ku Zambia pomwe dzulo wagoletsa zigoli ziwiri ndi kuthandizira zigoli zina ziwiri pomwe ZISD FC yagonjetsa National Assembly 4-1 mu FAZ National Women's Football League ku Zambia.
Katswiriyu tsopano ali ndi zigoli zisanu mu ligiyi pomwe ndi wachiwiri mu ndandanda wa atsikana omwetsa zigoli ndipo akutsogola pa ndandanda wa atsikana othandizira zigoli pomwe wathandizira zisanu chaka chino.
By Hastings Wadza Kasonga Jr
TEMWA SCORING FOR FUN IN CHINA
Scorchers forward, Temwa Chawinga, continues her impressive performances in China as her goal helped Wuhan Jiangda University beat Sichuan Women 2-0 in the China Women's Football League on Saturday.
Chawinga fired a shot from outside the box to double the scores and take her tally for the 2023 Season to 24 after playing 17 games for the team.
Meanwhile, Wuhan are on course of winning the league again for the fourth consecutive time as they lead the table with 42 points, 7 points clear on top.
Chawinga already won three golden boots awards only this year, two with Wuhan and another with Scorchers and is looking for her fourth in China.
Reported by Hastings Wadza Kasonga Jr
CHAWINGA SCORES FIRST PSG HAT TRICK
Scorchers forward, Tabitha Chawinga, has netted her first ever hat trick for PSG in France after helping the team to claim a 5-2 away win over Dijon on Sunday.
Chawinga netted one in the first half before completing her hat trick to claim a match ball in the second half with other goals coming from Geyoro and Vangsgaard in the match.
Chawinga has now five goals in the league, two behind the top goal scorer and its 6 goals for the team in all competitions in 6 games as well.
She joined the French side from Wuhan Jiangda University of Chinese Women's Football league on loan for a year.