Login with Facebook to post predictions, updates & live scores
"TITULUKANSO KU MBALI YA MATIMU OTULUKAWA" - KAFOTEKA
Mphunzitsi watimu ya FOMO FC, Elvis Kafoteka, wati timu yake ikadali ndi mwayi waukulu kuti ituluke ku chigwa cha matimu omwe atuluke mu ligi pomwe wati mmasewero omwe akutsalira awiri awathandizire kutero.
Iye amayankhula atatha masewero omwe agonja 1-2 ndi timu ya Civil Service United pa bwalo la Mulanje Park lamulungu pomwe wati ndi zopweteka kwambiri kugonja timu ikusewera bwino.
Iye watinso timuyi anayipeza ili ku chigwa cha matimu otulukawa ndipo anayitulutsa ndipo panonso ayitulutsa.
"Ndinayipeza ili komweku kale ndipo panonso ndiyitulutsa bola tingochita bwino mmasewero athu ndi Baka City lachitatuli komanso ena otsatira zikatero zitikhalire bwino, timu ilibwino kale, ikusewera bwino koma tikumangopanga kavuto pang'ono." Anatero Kafoteka.
Mmasewero otsatira, timuyi ikumana ndi timu ya Baka City yomwe yatsimikizika kuti yatuluka mu ligi ndipo iwo ali pa nambala 14 ndi mapointsi 22 pa masewero 24 omwe yasewera.
📷: Civo
Mutumize pa 0991509953
"BULLETS INASEWERA BWINO KOMA MPIRA SUKUYENDA BWINO" - KAMANGA
Mphunzitsi watimu ya Kamuzu Barracks, Charles Kamanga, wati timu yake yagonja chifukwa inakanika kuyigwira timu ya FCB Nyasa Big Bullets kuti isagoletse koyambilira komabe kayendetsedwe ka mpira sikali bwino mdziko muno.
Iye amayankhula atatha masewero omwe agonja 2-0 pa bwalo la Bingu ndipo wati anakonza kuti ayitchinge Bullets kuti isagoletse mu mphindi zoyambilira zenizeni koma zinavuta ndipo zinawabalalitsa.
Iye wati sakufuna kunamizira kugonjaku koma kusewera pafupifupi kukutopetsa osewera a timu yakeyi.
"Panopa zikuvuta chifukwa mpira tikusewera pafupifupi ndipo masiku 7 kusewera masewero atatu ndi zosagwira olo ku England sindikukhulupilira kuti zimachitika Izizi nde sikuti ndikunena kuti tagonja kamba ka izi koma zikufunika kuunikirapo." Anatero Kamanga.
Zateremu, timuyi tsopano yatuluka mu chikhochi ndipo FCB Nyasa Big Bullets yafika mu ndime yotsiriza ya chikhochi pomwe ikumane ndi Silver Strikers.
"ANALI MASEWERO OVUTA KWAMBIRI" - CHIDATI
Wachiwiri kwa mphunzitsi watimu ya Civil Service United, Wilson Chidati, wati masewero omwe timu yake inasewera ndi FOMO anali ovuta poti anzawowa akufuna kuti atsalebe mu ligi koma mwamwayi apeza chipambano.
Iye amayankhula atatha masewero omwe apambana 1-2 ku bwalo la Mulanje Park ndipo wati chipambano chimenechi chawathandiza kwambiri kuti afike patali kwambiri.
"Anali masewero ovuta kwambiri, ndimadziwa kuti FOMO ibwera mwamphamvu chifukwa choti ikufuna itsalebe mu ligi nde tinavutika koma mwamwayi tapeza mipatayo tagwiritsa ntchito." Anatero Chidati.
Kutsatira kupambanaku, timuyi yafika pa nambala yachisanu mu ligi pomwe ili ndi mapointsi okwana 38 pa masewero 25 omwe yasewera chaka chino.
Photo: Civo media
"TIDZASANGALALA MASEWERO ONSE AKADZATHA" - KAJAWA
Mphunzitsi watimu ya Bangwe All Stars, Trevor Kajawa, wati timu yake idzasangalala masewero onse akadzatha kuti adzatsimikize kuti atsala mu ligi pomwe wati nthawi ino ndi yomenyera nkhondo kuti itsalebe mu ligiyi.
Iye amayankhula atatha masewero omwe agonjetsa timu ya Moyale 1-0 pa bwalo la Balaka lamulungu ndipo wati timu yake inali ndi masewero ovuta poti Moyale Barracks ndi timu yabwino.
Iye wauzanso ochemerera atimuyi kuti chipambanochi ndi chiyambi cha zinthu zabwino kutimuyi ndipo ayesetsa kuti zikhale bwino.
"Mmene ligi yafikiramu zikufunika kuti tizipambana masewero nde sitisangaliratu koma tidikira kuti masewero onse athe kenako tidzasangalale chatsala ndi kulimbikira kuti tizichita bwino." Anatero Kajawa.
Timuyi ili pa nambala 13 mu ligi pomwe ili ndi mapointsi okwana 24 pa masewero 26 omwe yasewera chaka chino.
"KULUZA MASEWERO NDI ZAMPIRA" - MWANSA
Mphunzitsi watimu ya Moyale Barracks, Prichard Mwansa, wati timu yake inayesetsa kuti ichite bwino ndipo inakonza kuti ipambane mmasewero awo koma sizinayende ndi momwe anakonzera.
Iye amayankhula atatha masewero omwe agonja 1-0 ndi timu ya Bangwe All Stars lamulungu pa bwalo la Balaka ndipo wati timu yake inapeza mipata yochuluka kwambiri yomwe anakanika kugoletsa.
"Anali masewero abwino kwambiri tinapeza mipata kuti mwina tikanatha kupeza zigoli koma tinakanika komabe zimachitika mu mpira tibwerera tikakonze mavuto athu kuti tipitilire kuchita bwino." Anatero Mwansa.
Moyale Barracks ili pa nambala yachisanu ndi chimodzi (6) pomwe ili ndi mapointsi okwana 36 pa masewero 26 omwe yasewera mu ligi ya chaka chino.
Maxwell
BULLETS IKUMANA NDI SILVER LOWERUKA
Matimu a FCB Nyasa Big Bullets komanso Silver Strikers akumana mu ndime yotsiriza ya chikho cha Airtel Top 8 kutsatira kupambana masewero awo amu ndime ya matimu anayi a mpikisanowu.
Timu ya Bullets inagonjetsa Kamuzu Barracks 2-0 pa masewero omwe anaseweredwa lamulungu pa bwalo la Bingu ndi zigoli za Ephraim Kondowe komanso Blessings Mpokera.
Ndipo timu ya Silver Strikers inadalira chigoli cha Binwell Katinji kuti igonjetse Mighty Mukuru Wanderers 1-0 loweruka kuti ikhale yoyamba kufika mu ndimeyi.
Bungwe la Football Association of Malawi lalengeza kuti ndime yotsirizayi iseweredwe loweruka pa 09 November 2024 pa bwalo la Bingu lomweli nthawi ya 3 koloko masana.
Wolemba: Hastings Wadza Kasonga Jr
Ikanakhalaso ya 5pm
"WE ARE LACKING A LEADER" - PASUWA
FCB Nyasa Big Bullets head coach, Kalisto Pasuwa, says his team is failing to be consistent in their performances this season as they lack a leader who can be talking to the boys in the game.
He said this ahead of their Airtel Top 8 semi final match against Kamuzu Barracks at the Bingu National Stadium and said if there was a leader who can be communicating to the boys in their matches they can do better.
He further said against Premier Bet Dedza Dynamos, they thought the presence of Clyde Senaji could bring changes but they were attacked now and then. He also said his team is missing too many chances.
"We need to work with our last third of attack you saw on Thursday we were missing many chances getting into the box we miss the chance we come again we keep on missing then the opponent comes once then we are punished and also after being punished the response will also be down yes we have been scored we need to look up and play football and look
for that equaliser or a winner of the day so its also character that makes us also to win games." Said Pasuwa.
Meanwhile, the winner of the match will play Silver Strikers in the final of the tournament after the Bankers beat Mighty Mukuru Wanderers 1-0 on Saturday afternoon.
CHITIPA IKUYANG'ANIZANA NDI KHOMO LOTULUKA MU LIGI
Timu ya Chitipa United ikuchepetsabe mwayi wawo wotsala mu ligi ya TNM pomwe yagonja pakwawo 1-3 ndi timu ya Mzuzu City Hammers very pa masewero omwe anaseweredwa pa bwalo la Karonga lamulungu masana.
Promise Ogboaza anatsogoza Hammers pa mphindi 28 asanabwere Chimwemwe Chunga pa mphindi 44 koma Ramadan Ntafu anabwenza chimodzi pa mphindi 51 ndipo Gregory Mwase anagoletsa chigoli chachitatu pa mphindi 86 kuti Hammers iweruke bwino.
Mphunzitsi watimu ya Chitipa United, Christopher Nyambose, wati timu yake sinasewere bwino mmasewero awo zomwe zinapangitsa kuti akanike kupambana pa masewero awo.
"Anali masewero ovuta kwambiri, tinawapatsa ulemu anzathuwa poti mwina ndi anzathu akumpoto kuno komanso odziwana nawo nde timayesa kuti sabwera mwamphamvu koma masewero alero nde sitinasewere bwino." Anatero Nyambose.
Timuyi ili pa nambala yachikhumi ndi chisanu (15) pomwe ili ndi mapointsi 19 pa masewero 25 omwe yasewera mu ligi ya TNM.
KUMWEMBE SCORES IN BUFFALOES WIN
Malawian forward, Christopher Kumwembe, was on target as Green Buffaloes beat Mutondo Stars 1-4 in the MTN Super League in Zambia on Sunday afternoon.
The towering forward opened the scores on 45th minute in the first half before Eric Choma, Golden Mashata and Perkins Mumba Mwale scoring a goal each in the second half while Titus Chansa netted the consolation goal for the hosts.
This marks Christopher Kumwembe's second goal for the team in Zambia where he is playing on loan from Mighty Mukuru Wanderers.
Reported by Hastings Wadza Kasonga Jr
BREAKING
Bangwe All Stars has moved out of the TNM Super League relegation zone after beating Moyale Barracks 1-0 at the Balaka Stadium on Sunday.
Kondwani Chilembwe scored the much needed goal on 76th minute of the game to seal the win for the Blantyre based side.
However, the team has also to praise Civil Service United which sealed a comeback 1-2 win over FOMO FC to enable Bangwe move out of the red line for the first time in almost 5 months.
Bangwe All Stars are now 13th on the log table with 24 points from 26 games in the League, two points ahead of FOMO FC which also has two games in hand.
2-2 in 90min
Bangwe 1-0
BAKA SAYS THEY ARE TIRED OF LOSING
Baka City assistant coach, Davie Kayira, says his team is very tired of losing and they will just finish their remaining games in order to start all over again in the Northern Region Football League with the hope of returning to the elite League in 2026.
He said this after the team lost 2-3 on post match penalties to non League side, Hilltop FC after a 1-1 draw in the 90 minutes at the Karonga Stadium on Saturday and said his team lost because they underrated their opponents.
He further said that his team needs to be rebuilt when they go to the lower but as for now, things are worse than before.
"I think there's nothing more left here, we are tired of losing and what will do is to just finish our games so that we go back to the lower league and maybe we may come again next year." Said Kayira.
Indeed the team deserved to get tired of losing as they have lost 19 of their 25 games in the League as they have managed a win and five draws in the curren
"TILEMBA MBIRI YATSOPANO YOMWE ANTHU ATADABWE" - KAMANGA
Mphunzitsi watimu ya Kamuzu Barracks, Charles Kamanga, wati anyamata ake akonzeka kwambiri kuti apange mbiri yomwe sinachitikepo pomwe akufuna afike mu ndime yotsiriza ya Airtel Top koyamba lamulungu.
Iye amayankhula patsogolo pa masewero awo ndi timu ya FCB Nyasa Big Bullets mu ndime ya matimu anayi a mpikisanowu ndipo wati timu yake yakonzeka bwino mmasewerowa.
"Takonzekera bwino kwambiri kuti mwina tichite bwino pa masewero amenewa tikudziwa kuti akhala masewero ovuta poti tikusewera ndi timu yabwino koma ndime ngati iyiyi ndi yomwe timayesetsa kuti tichite bwino nde anyamata akonzeka." Anatero Kamanga.
Iye wati katswiri wawo womwetsa zigoli kutimuyi, Zeliat Nkhoma sapezeka mmasewerowa kamba kovulala koma onse alibwino kutimuyi.
Timu yomwe ipambane pa masewerowa idzakumana ndi timu ya Silver Strikers mu ndime yotsiriza ya mpikisanowu yomwe yagonjetsa Mighty Mukuru Wanderers loweruka.
FC Nyasa 2-1 Kamuzu Barracks
Napoli
Manoma forever 😍
Power 🏁
"TATSALA NDI LIGI KOMANSO CASTEL" - MWASE
Mphunzitsi watimu ya Mighty Mukuru Wanderers, Meke Mwase, wati tsopano timu yake ikuyenera kulimbikira mu zikho ziwiri zomwe atsalamo mu ligi ya TNM komanso chikho cha Castel kuti mwina chaka chino achimalizeko bwino.
Iye amayankhula atatha masewero omwe agonja 1-0 ndi timu ya Silver Strikers ndipo atuluka mu ligiyi ndipo wati timu yake ikuvutika ndi vuto logoletsa zigoli zachangu kwambiri.
"Anali masewero ovuta kwambiri, vuto ndi loti sitinayambe bwino mchigawo choyamba, tinachinyitsa mofulumira koma tinayesetsa kubweramo tasewera bwino koma mwina chifukwa cha phuma sitinathe kupeza zigoli." Anatero Mwase.
Iye watinso timu yake iyesetsa kukonza mavuto awo kuti mmasewero omwe akudzawa ayende bwino pomwe tsopano akanika kupambana Airtel Top 8 komanso FDH Bank.
Timu ya Silver Strikers inagoletsa chigoli chawo pa mphindi zisanu ndi zitatu (8) kuti atulutse Wanderers yomwe inali ikusewera bwino kwambiri
Who is red carded
KABZERE SCORES ON DEBUT
Scorchers Youngster, Rose Kabzere, has scored her first goal for Montpellier in France as the team beat Guingamp 7-0 in the Arkema Premier League on Saturday afternoon.
Kabzere was put in the team's match day squad last week and was introduced on 70th minute of the game before assisting the 6th goal on 75th minute and netted her own on 81th minute.
She is the second Malawian to play in the French league after Tabitha Chawinga who plays for Olympic Lyonnais .
"CHIPAMBANO TACHIPEZA MOVUTIKIRA" - MPONDA
Mphunzitsi watimu ya Silver Strikers, Peter Mponda, wati timu yake yapambana koma movutika kwambiri pomwe timu ya Mighty Mukuru Wanderers inawapanikiza kwambiri pa masewero awo.
Iye amayankhula atatha masewero omwe agonjetsa Manoma 1-0 pa bwalo la Bingu mu mzinda wa Lilongwe ndipo wati timu yake inachita bwino mu mphindi 35 zokha pa masewerowa.
"Anali masewero ovuta kwambiri ifeyo tinakwanitsa kusewera bwino my mphindi 35 zoyambilira koma kwinako Wanderers inatipanikiza, tinali ndi mipata ingapo koma sitinagwiritse ntchito ngakhale timavutika nde sinnasangalale ndi kaseweredwe koma zotsatira ndi mmene anyamata anaikira mtima." Anatero Mponda.
Iye wati sakusamala kuti akumana ndi timu yanji koma chomwe akupanga panopa ndi chisangalalo basi kudikira kuti mtsiku la lamulungu itapambane ndi chani.
Chigoli cha Binwell Katinji mu mphindi zisanu ndi zitatu za masewero ndi zomwe zathandizira kuti timuyi ifike mu ndime yotsiriza ya mpikisano wa Ai
Log table plz plz pzl
Why you don't show log table of top 12?
Chifundo kamwana
GAMPHANI RESCUE BULLETS AGAINST FAMILIAR STRANGERS
Super Substitute, Lameck Gamphani, netted a 96th minute equaliser to deny his former team, Premier Bet Dedza Dynamos their first away win of the season as FCB Nyasa Big Bullets played a 1-1 draw at the Kamuzu Stadium on Thursday afternoon.
Babatunde Adepoju saw his penalty kick brilliantly saved by Donnex Mwakasinga in the first half before Substitute Ibrahim Sadick fired the hosts ahead when Marco Chiwaya did well to challenge Gomegzani Chirwa but Gamphani had to come off the bench to rescue the Palestinians in hands of his former side which had a man less following the red card of Khumbo Banda on 81st minute.
Head coach for the People's team, Kalisto Pasuwa, said his team missed a lot of chances leading to their struggle in the match.
"You could see the body language in some of the players the way we were playing unfortunately we got our chances but we could utilize them and the opposition got one and they punished us and most of
the second half they were leading us we tried as much as we can looking an equaliser and we got it in the last minute." Said Pasuwa.
The People's team remain third but now add a point to 41 points from 24 games, 6 points behind second placed Mighty Mukuru Wanderers and 13 points behind leaders, Silver Strikers.
PASUWA DOWNPLAYS FLAMES JOB LINKS
FCB Nyasa Big Bullets head coach, Kalisto Pasuwa says he can not comment on the rumours linking him to Flames coaching role as he is an FCB Nyasa Big Bullets coach not Flames coach.
The Zimbabwean said this on Wednesday during a media briefing ahead of his team's match against Premier Bet Dedza Dynamos on Thursday at the Kamuzu Stadium.
He said it is hard to speak on things he does not know and not being even approached by Football Association of Malawi.
"I think it is hard for me to comment on rumours and things I dont know and even I have never been approached for that so what I know is that I'm working at Bullets so I can't comment." Said Pasuwa.
Meanwhile, the five time TNM Super League winner had ever been assigned a job by the football governing body as he was assigned to lead the Under 23 National team.
KAMUZU BARRACKS MATCH INTO CASTEL R16
Elite League side, Kamuzu Barracks, has become the fourth team to book a place in the round of 16 of the Castel Challenge Cup 2024 edition after beating Ntchisi Tigers 4-0 at the Nankhaka Stadium on Wednesday afternoon.
Gregory Nachipo put the Soldiers ahead on 13th minute before Redson Nkhoma doubling the scores from a free kick four minutes later as the hosts led 2-0 at half time. Substitute Sheriff Maulana won a penalty which Nkhoma converted for his second of the day on 64th minute before Maulana himself finding the back of the net with a powerful shot on 85th minute.
After the game, head coach for the Soldiers, Charles Kamanga thanked his boys for the win but said his team could have scored more than four in the match.
"It was a tough game but we have managed to win, I think we were underrating our friends because we could have easily scored more than four goals but I thank the boys for the win." Said Kamanga.
The result means Kamuzu Barr
"WE STRUGGLE WITH THE SO-CALLED SMALL TEAMS" - PASUWA
FCB Nyasa Big Bullets head coach, Kalisto Pasuwa, says his team needs to be positive enough in order to get past Premier Bet Dedza Dynamos on Thursday as his team is struggling much with the so-called small teams in the League.
He said this ahead of their match against the Dedza based side at the Kamuzu Stadium and said there's a problem where if his team win the Derby, some players feels they will not sweat for results in other games.
"if you look at these teams like Dedza and those ones that can be called small teams are those that are giving us problems but one thing I can say is the mental part of it where we go to a game where we think everything is easy." Said Pasuwa
He however said his team is already prepared on mindset on this game and that his team will not looking at what other teams are doing but their own performance and see on the last day of the League.
The People's team is third on the league standings with 40 p
"WE ARE STILL LOOKING FOR AN AWAY WIN" - BUNYA
Premier Bet Dedza Dynamos head coach, Andrew Bunya, says his team is itching for their first away win in the TNM Super League and their match against FCB Nyasa Big Bullets is one of those they will to record one.
He said this ahead of their match on Thursday at the Kamuzu Stadium and said his team is ready as they need more points to fight for top 8 positions in the League.
"We are prepared for the game and our boys are looking in good shape, tactically and mentally they are looking good. We are still fighting hard to that we get wins more especially an away win so this is also one of the games that we are looking forward to." Said Bunya.
A win will take the team at a more safe place in the League as they will rise to 32 points as they are now on 29 points from 24 games on 11th position.
Blue eagles 0-1 Namitete Zitha
Namitete Zitha will.win today match
"TANGOWAPATSA ZIGOLI LERO" - IKWANGA
Mphunzitsi watimu ya Mzuzu City Hammers, Kondwa Ikwanga, wati ndi wokhutira ndi mmene timu yake yasewerera ndi Silver Strikers koma zangovuta kuti amasewera ndi timu yodziwa mpira yomwe anakanika kuyigoletsa kenako nkupereka zigoli.
Iye amayankhula atatha masewero omwe agonja 0-2 ndi timu ya Silver Strikers pa bwalo la Mzuzu ndipo wati ngakhale iwo agonja koma asewera bwino kwambiri.
"Anali masewero abwino koma tapereka zigoli lero chifukwa tinakonza kuti tipeze zigoli zachangu koma timasewera ndi timu yabwino komabe ndine wosangalala poti timatha kupita kutsogolo kusiyana ndi kale lija lomwe timangokhala mu chigawo chathu." Anatero Ikwanga.
Iye wati timu yake imaliza mu matimu atatu oyambilira mu ligi ndipo anthu asakayike poti ali kale momwemo.
Timuyi ikadali pa nambala yachinayi mu ligi pomwe ili ndi mapointsi okwana 40 pa masewero 26 omwe yasewera mu ligi ya TNM.
"I'M HAPPY WITH THE RESULT NOT PERFORMANCE" - MPONDA
Silver Strikers head coach said he was happy after seeing his team return to winning ways in the TNM Super League but was not pleased with their performance only that they agreed to force a win in Mzuzu.
He said this after the team's 0-2 win over Mzuzu City Hammers at the Mzuzu Stadium on Saturday afternoon and thanked his boys for the win.
"I'm happy with the result but not with the performance, it was not that good today but after the draws we agreed that we should force a win and in the first half we created few chances which we missed and in the second half we created many and got the goals." Said Mponda.
He further said that at least things are working on their side as they are remaining with 6 games leading with 7 points on the log table.
The Bankers have now 54 points in the League from 24 games they have played this season.
NKHOMA, MWAUNGULU ON TARGET IN BIG WIN
Flames attackers, Patrick Mwaungulu and Lanjesi Nkhoma were on target as Don Bosco beat Group Basano 4-1 in DRC on Wednesday afternoon.
Nkhoma finished off a brilliant goal in the first half for the team's opener while Mwaungulu netted a beauty outside the box for the team's third goal in the match.
This was Nkhoma's first goal in two games he has played for his team while Mwaungulu makes it two goals in two games for the team.
"TIKANAMENYERA PA CIVO TIKANACHITA BWINO" - CHIDATI
Mphunzitsi watimu ya Civil Service United, Wilson Chidati, wati timu yake ikanatha kuchita bwino ikanakhala kuti imasewera pa bwalo la Civo ndipo kusintha komwe kunalipo kwawasokoneza kwambiri.
Iye amayankhula atatha masewero omwe agonja 1-3 ndi timu ya Creck Sporting Club pa bwalo la Champions masana a lachitatu ndipo wati anyamata ake anali obalalika kwambiri.
"Anali masewero abwino koma tsiku la lero anyamata anali wobalalika ndi zomwe zachitika angakhale ifenso tinabalalika nde tingowayamikira anzathu kuti asewera bwino." Anatero Chidati.
Timuyi inali pa mkangano ndi bungwe la Super League of Malawi pomwe iwo amafunabe kuti masewero aseweredwe pa bwalo la Civo osati ku Champions koma bungweli linakulabe mphamvu.
Timuyi tsopano yatsika pomwe ili pa nambala yachisanu ndi chiwiri (7) pomwe ikadali ndi mapointsi okwana 35 pa masewero 24 mu ligi.
"MPIRA UTHA KUMUPHA MUNTHU NDITHU" - NYAMBOSE
Mphunzitsi watimu ya Chitipa United, Christopher Nyambose, wati zomwe waziona tsiku la lero sanazionepo ndipo zikhonza kupha munthu pomwe goloboyi wawo walakwitsa kawiri kuti Mighty Mukuru Wanderers ipambana 1-2 ndi timu yake.
Iye amayankhula atatha masewero omwe anali pa bwalo la Karonga ndipo wati masewero awa ndi opweteka poti angowapatsa a Wanderers zigoli.
"Ndi zopweteka kwambiri ndipo mpira utha kuphadi munthu chifukwa zomwe zachitika panopa sinnazione chifukwa lero nde tataya masewero owinawina komabe goloboyi poti ndikoyamba kugwirira Supa ligi timanjenje koma zapweteka kwambiri." Anatero Nyambose.
Iye wati masewerowa akanathandiza timuyi kuti ifike pa nambala 13 mu ligi koma zateremu zavuta komabe wati chaka cha mawa adzakhala akuphunzitsabe timuyi mu ligi yomweyi.
Iwo akadali pa nambala 15 mu ligi pomwe ali ndi mapointsi okwana 19 pa masewero 24 omwe yasewera mu ligi.
WANDERERS RETURN TO WINNING WAYS
Mighty Mukuru Wanderers are back to winning ways after the team sealed a comeback 1-2 win over Chitipa United to end their two game loss in the TNM Super League on Wednesday.
Gaddie Chirwa's long range cancelled out a Rajab Nyirenda's opener before goalkeeper Davie Ndili punching the ball from Wisdom Mpinganjira into his own net to seal a comeback win at the Karonga Stadium.
Head coach, Meke Mwase thanked his boys for working extra hard to seal the much needed win.
"We are happy to win this game and today's workrate of the boys was good, we had a very good first half which we failed to score and in the second half, we conceded a goal but the boys tried and we won the game." Said Mwase.
He has however said the team will not stop pushing as everything is still there and it is not over for them.
The Nomads are still second on the log table with 47 points from 24 games in the League, 7 points behind leaders Silver Strikers.
KAMWENDO SENDS CRECK BACK INTO TOP 8
Creck Sporting Club have moved from number 10 to position 6 in the TNM Super League log table after the team recorded a 1-3 win over Civil Service United with Joseph Kamwendo in charge in a match played at the Champions Stadium on Wednesday afternoon.
George Chaomba scored twice on either side of Damiano Kunje's goal before Muhammad Sulumba sealing the win in the second half as the rookies returned to winning after staying for many weeks without a win under the suspended Macdonald Mtetemera.
Interim coach, Joseph Kamwendo, thanked his boys for playing according to their plan.
"We are very happy for the win I think the boys played according to our plan, we knew it was going to be a tough game as we were also playing away but our approach in this game was positive from the word go." Said Kamwendo.
Following the win, the team are now 6th from 10th in the League as they have 35 points from 24 games played this season.
Reported by Hastings Kasonga
all groups
scochars