Login with Facebook to post predictions, updates & live scores
BB MOTOMOTO
congratulation savenda chitipa united
Game yomwe inayenera kukhalapo lero pa 19 May 2019 Ku Nchalo Mechanical pool stadium yalephereka chifukwa team ya factory rangers ili ndi mulandu.
Congras nyasa
Nyasa big bullets vs civo results
All results updated now.
Timu yampira wa miyendo ya dziko lino lero, Lamulungu ikuyamba kuchita zokonzekera zake patsogolo pa mpikisano wa Cosafa.
Meke Mwase waitana osewera omwe akuyembekezeka kuyamba zokonzekera-zi.
Hangover vs Chinamwali Stars game will be played at Moneymen Ground @ 2:30 PM CAT.
BB AND THEIR RESERVE MUST MOVE BACK TO THE PLACES THEY BELONG.
Tnm super league 2019
ss2:ms1
noma yomweyo kuti wawa
Fish Eagles has withdrawn participation in the SIMSO League due to problems beyond their reach as such all points other teams accumulated are declared null and void.
Civil Sporting yati ikudziwa kuti masewero awo a m'chigawo cha kumwera akhala ovuta koma ali ndi chikhulupiliro kuti abwerako ndi mapoint onse 6.
BB 1 - Civil 0
Wanderers yatsutsa malipoti oti yasiya osewera ena monga mmene anthu akunenera pa masamba a mchezo a intaneti.
Anthu ena akufalitsa kuti timuyi yasiya Alfred Manyozo komanso Harry Nyirenda kumpoto.
Timu ya BE FORWARD Wanderers ili m'chigawo cha Kumpoto komwe ikuyembekezeka kusewera masewero awiri.
Albert Mpinganjira, mphunzitsi wa timuyi wati achita chotheka kuti apambane masewero awo onse.
Tapedza kale 3points yasala inayo tikuifunabe
2019
FIFA legend and former Nigerian International, Yakubu Ayegbeni is today expected to visit Chikwawa and Nsanje districts.
Ayegbeni will assess damage caused by floods on sports infrastructures.
Yamikani Chester scored his first goal for North Carolina. Chester came from the bench to help his team win 4-1.
Reports reaching Owinna indicates that BE FORWARD Wanderers has fired Yasin Osman and Allan Kamanga.
The duo, and Bob Mpinganjira were on suspension.
blessings
Mitundu 2 enawo o
karonga 1-2 wanderers
wanderers 2-0 chitipa
Blue Eagles in the next three days will be involved in a massive awareness campaign on protection of people with albinism.
The Team will travel to Mchinji, Machinga and Nsanje.
Zikufunika kumaka
Hackman
Teams that have reached Airtel Top 8 semi finals; Silver Strikers, Mzuni, Karonga United and Masters Security.
Masters Security and Silver Strikers are through to the semi finals of Airtel Top 8.
Karonga United XI: Munthali, Thulu, Mwalwimba, Mwenenguwe, Mwakifuna, Malema, Lungu, Mfune, Msowoya, Mwaluswa, Selemani.
Timu ya Malawi isewera masewero ake oyamba mu mpikisano wa Cosafa ndi Seychelles.
Masewero-wa azaseweredwa pa 26 mwezi uno.
Noma lero wamkaka basi 3-1
For show
Saturday fixtures
Chipiku Division 1 fixtures updated https://owinna.com/mwicr/cr...
Silver Strikers and BE FORWARD Wanderers will play 3 games each in a space of 6 days.
The teams start their 3 games challenge tomorrow as they meet at Silver Stadium.
Ntopwa has collected its first 3 points in the northern region over the weekend.
The team won against Savenda Chitipa United with 3 goals to 1.