Login with Facebook to post predictions, updates & live scores
Wanderers 2 0 Sirver
Timu ya Mzuni yapitilira mu ndime ina mu mpikisano wa Airtel Top 8 kutsatira kulepherana ndi Civo pogoletsana chigoli chimodzi ali yense.
Starting XI of Karonga against Ntopwa: Munthali, Thulu, Mwalwimba, Mwenenguwe, Mwakifuna, Malema, Lungu, Mfune, Msowoya, Mwaluswa, Selemani.
Mtedza plays 5games 12points not 9
Game ya Mtedza vs Machinga ADD on Sat 27 April inaseweredwa? What's the result?
2 -0
Thums up premier league log table
ThumbsUp Premier Division log table: https://owinna.com/mwisr/sr...
Supper league
Premier league
Timu ya mpira wa miyendo ya dziko lino, Flames, yatuluka mu mpikisano wa CHAN kutsatira kulepherana ndi Eswatini pogoletsana chigoli chimodzi ali yense.
Yinthele 0-0
Mphunzitsi wa Savenda Chitipa United wadandaula kaamba kosasewera masewero ena ali onse mu ligi kwa sabata ziwiri.
Flames to host Eswatini at Kamuzu Stadium in second leg game of CHAN competition. One word for Malawi's coach, Meke Mwase.
Flames coach, Meke Mwase says Chikoti Chirwa, Alfred Manyozo, Peter Banda, Dennis Chembezi and Peter Cholopi will miss today's game due to injuries.
Chimango Kaira has joined his fellow players in Flames camp replacing Chikoti Chirwa.
Chirwa has sustained an injury.
Chikoti Chirwa might play for Kamuzu Barracks after being transferred by MDF from Zomba to Kamuzu Barracks offices.
Mighty Tigers will this morning depart to Lilongwe where they will battle it out with Mlatho Mponela and TN Stars.
Robin Abambo Alufandika said they are optimistic of collecting all points.
Malawi National Football Team head coach, Meke Mwase, says his charges are fully prepared for tomorrow's game against Eswatini.
B FOWARDI WADRAS
Nyasa Big bullets
Max guzza banda
Otsatira timu ya Wanderers dzulo abwereza kuuza akuluakulu oyendetsa timuyi kuti achotse aphunzitsi onse.
Otsatira timuyi amanena izi pomwe anagonja ndi timu ya Blue Eagles pa bwalo la Kamuzu.
Phangala yosewera pakati mu timu ya Wanderers, Joseph Kamwendo, wabwera mdziko muno kuchokera kunja komwe amasewera.
Kamwendo anaoneka dzulo pa bwalo la Kamuzu pomwe timu yake, Wanderers, yaluza.