Masewero a Silver ndi Wanderers apititsidwa pa Bingu
Bungwe la Super League of Malawi lalengeza kuti masewero a pakati pa Silver Strikers FC komanso Mighty Wanderers FC asunthidwa kuchoka ku bwalo la Silver kupita ku bwalo la Bingu.
Bungweli lalengeza za izi lachitatu masana pomwe tsiku losewerera pa masewerowa lomwe ndi pa 22 November 2025 silinasinthe.
Matimuwa akumanako katatu mu zikho zonse chaka chino ndipo ku mphindi 90 akhala akulepherana komano Silver yapambana kawiri pa mapenate mu zikho ziwiri.
Login with Facebook to post predictions, updates & live scores