Timu ya Ekhaya FC yatsimikiza kuti yalekana ndi katswiri wawo wosewera pakati Chimwemwe Yassin yemwe wathetsa mgwirizano wake.
Yassin yemwe anasewerakonso matimu a FCB Nyasa Big Bullets Reserve komanso Bangwe All Stars wachita izi kamba koti nthawi yake yosewera imachepa.
Timuyi yamufunira zabwino zonse pomwe akupita ku matimu ena amu ligi ya TNM.
Login with Facebook to post predictions, updates & live scores