Timu ya FCB Nyasa Big Bullets yasaina katswiri wotseka kumbuyo kutimu ya Creck Sporting Club, Aaron Chilipa, pa ngongole ya miyezi isanu ndi umodzi.
Timu ya Creck Sporting Club ndi yomwe yatsimikiza za Kuchoka kwa mnyamatayu yemwenso amavutika kuti apeze nthawi yosewera kutimuyi.
Chilipa anasewerapo timuyi mmbuyomu pomwe ankasewera timu ya Reserve ya timuyi.
Login with Facebook to post predictions, updates & live scores