Mphunzitsi watimu ya Flames Kalisto Pasuwa wayitana Charles Petro kuti akhale nawo mu gulu la osewera omwe atumikire timuyi mu masewero opitira ku World Cup.
Timu ya Katswiriyu ya FC Botosani ndi imene yatsimikiza za nkhaniyi kudzera pa tsamba lawo la mchezo.
Login with Facebook to post predictions, updates & live scores