NKHANI
Timu ya FOMO FC yachotsa goloboyi wawo, Noel Phiri, yemwe wauzidwa kuti sali bwino ndipo sakufunikiranso kutimuyi.
Izi zadziwika pomwe katswiriyu watsimikiza kuti timuyi yamulembera kalata kuti athana naye.
Phiri ndi mmodzi mwa osewera omwe ayilowetsa timuyi mu ligi ya TNM pomwe anali pagolo pa masewero omwe timuyi inagonjetsa Ntopwa FC chaka chatha kuti ilowe mu ligi yaikuluyi.
Login with Facebook to post predictions, updates & live scores