Login with Facebook to post predictions, updates & live scores
David Banda who was adopted by Madonna is now playing for Benfica FC reserve side.
Best midfielder for 2019 season, Micium Mhone, was born today.
Mhone plays for Blue Eagles.
#HappyBirthDay #Mhone #AgeWithGrace #Zampira
Mkulu wa timu ya Ntopwa, Isaac Jomo Osman, wati mu season ya 2020 agwilitsa ntchito osewera achisodzera.
Osman wati achita izi pofuna kupereka mwayi kwa osewera-wa kuti aonetse luso lawo.
Gabadinho Mhango on Saturday scored his 12 goal in Absa Premier League, South Africa.
Mhango helped his team, Orlando Pirates win 3-1 against Highlands Park.
In Malawi player of the season, Peter Banda, received 300,000 Kwacha whilst in Mozambique, 2019 player of the season received a car.
#Zampira
Bungwe la FAM pamodzi ndi kampani ya FISD ati posachedwapa akhale akupereka mphoto kwa matimu komanso osewera omwe anachita bwino mu mpikisano wa FISD chaka chatha.
Kusowa kwa mgwirizano ku timu ya Wanderers ati ndiko kukupangitsa kuti mavuto apitilire kukuta timuyi.
Mlembi wa masapota wa Wanderers, Samuel Mponda, ndiye wanena izi.
Akuluakulu a Wanderers awapempha kuti afulumizitse kuchititsa chisankho ku timuyi.
Mlembi wa masapota wa timuyi, Sammuel Mponda, ndiye wapereka pempholi.
Zikukaikitsa ngati TNM ionjezere ndalama za ligi yaikulu ya m'dziko muno pomwe mkulu wa kampaniyi pa mwambo opereka mphoto ku Blantyre sanayankhulepo za izi.
Chikumbutso Kanyenda has shown interest to join Civil Sporting in 2020 season as he wants to undergo trials at the club.
Chikumbutso is the son to former Flames striker, Esau Kanyenda.
Good to go here in Blantyre at Mount Soche.
2019 best performing teams and players to receive their awards.
World Cup Qualifiers have moved from March/ June to October/ November.
AFCON Qualifiers have moved from September/October/ November to March/June /August/September.
Ma bwalo a Chilomoni komanso Mpira Village akhala oyamba kugwilitsa ntchito njira ya makono yolipilira, E ticketing m'chingerezi.
Mtsogoleri wa bungwe la FAM, Walter Nyamilandu, ndiye wanena izi.
Masapota apempha akuluakulu a Wanderers kuti achititse msonkhano waukulu patsogolo pa chisankho ku timuyi.
Sylvester Luka wati pa msonkhano-wu akuyenera kukambirana za mavuto omwe akuta timuyi.
2020 TNM Super League will commence in March this year.
This has been communicated by FAM officials in press statement released on Thursday.
The league will come to an end on 20 December.
FAM Charity Shield is scheduled to take place on 14 March.
This has been agreed by FAM executive members at the meeting they held in Mangochi.
Date and venue will be announced in due course.
Denis Chembezi has been offered a two and half year contract by Polokwane City in South Africa.
This has been confirmed by officials at the club.
Facebook
Timu ya Silver Strikers yati ikhale ikutchula mphunzitsi wake wa tsopano mu February.
Wapampando wa timuyi, Chiku Kalilombe, ndiye wanena izi pomwe wati amaliza kuchita mayeso a ntchitoyi.
Gabadinho Mhango yesterday helped Orlando Pirates win against Sundowns 1 nil.
Gaba scored the goal at 30 minutes.
He now leads in the league with 11 goals.
Gabadinho Mhango is now called CR 7 by Orlando Pirates supporters as girls are offering themselves for marriage.
Timu ya Civil Sporting iyamba zokonzekera zake pa 18 February.
Mphunzitsi wa timuyi, Eliah Kananji, watsimikiza za nkhaniyi.
Malingana ndi a Kananji akuyembekezera kuti aonjezera wosewera ena.
Mphunzitsi wakale wa timu ya Moyale Barracks, Charles Kamanga, watsutsa malipoti oti wasankhidwa kukhala mphunzitsi wa Ekwendeni Hammers.
Malingana ndi Kamanga, timu ya Ekwendeni sinamufikire.
Pali mwayi waukulu woti Khuda Muyaba atha kusewerera timu yina yaku Portugal pomwe zokambirana ati zafika ku mapeto.
Mlembi wa Silver Strikers, Innocent Kadamanja, watsimikiza za nkhaniyi.
Blue Eagles will soon start playing friendly games with district select teams to disseminate the importance of having community policing in their areas.
Red Lions will commence 2020 preparations on 5 February.
Coach for the club, Nelson Chirwa, has confirmed the development to Owinna.
According to Chirwa they are expected to recruit some players .
Timu ya Liverpool ikufuna wosewera waku Malawi wa zaka 17.
Wosewera-yu dzina lake ndi Henri Kumwenda.
Pakadali pano Kumwenda akusewera timu ya Leeds Academy.
One of the renowned sports commentators, Humphreys Mvula, says the issue of politicising BE FORWARD Wanderers is leading to the team's poor perfomance.
Malipoti akusonyeza kuti wosewera wakale wa timu ya Bullets komanso Masters Security, Kondwani Schores Kumwenda, atha kusewera timu ya Sable Farming chaka chino.
Bungwe loyendetsa masewero a mpira m'dziko muno la FAM, lichititsa mkumano wake oyamba Lachitatu likudza-li.
Mkulu ofalitsa nkhani ku bungwe-li, Gomegzani Zakazaka, watsimikiza za nkhaniyi.
NRFA will this coming Saturday hold its 2019 award ceremony.
One of the officials of NRFA, Ollens Msonda, has confirmed the development to Owinna.
Flames Captain, John CJ Banda, is expected to leave the country for Mozambique.
Acccording to Blue Eagles media officer, Steve Kumalonje, Banda will play along side Schumacher Kuwali at UD Songo.
Flames and Nyasa Big Bullets defender, Charles Petro is set to attend trials in Moldova.
The youngster is expected to attend trials at Sherif Tiraspol a team playing in the country's elite league.
Kampani ya Nyasa Manufacturers yati izithandiza timu ya osewera akale a timu ya Nyasa Big Bullets.
Mkulu wakale wa timuyi, Fleetwood Haiya, ndiye wanena izi kutsatira kukhazikitsidwa kwa timuyi.
FAM President, Walter Nyamilandu, was in NkhataBay attending the burial of his uncle.
Owinna would like to send condolences to the FAM boss.
#MHSRIP
Ntopwa will start its 2020 football preparations on 3 February.
Technical Director for the club, Isaac Jomo Osman, has confirmed the development.