Login with Facebook to post predictions, updates & live scores
Prolific forward Schumacher Kuwali leaves the country for Mozambique tomorrow where he is set to start a new lease of life with UD Songo.
Steve Madeira waonetsa chidwi chopikisana nawo pa chisankho cha Wanderers mu February.
Malingana ndi Madeira wapanga chiganizo-chi kutsatira kusachita bwino kwa Wanderers mu 2019.
Mphunzitsi wa timu ya Blue Eagles, Declerck Msakakuona, wati khumbo lake mu chaka cha 2020 ndi kutenga ukatswiri wa ligi ya TNM.
Mphunzitsi-yu wanena izi poyankhula ndi Owinna.
Score
Reports indicate that Flames captain, Christopher Banda, might play 2020 football season in South Africa.
This follows the expiry of the loan deal he had with UD Songo in Mozambique.
Akuluakulu a Wanderers ayelekeza pa 8 February ngati tsiku lomwe achititse chisankho ku timuyi.
Wapampando wa timuyi, Gift Mkandawire, watsimikizira Owinna za nkhaniyi.
Wosewera kumbuyo kwa timu ya BE FORWARD Wanderers, Denis Chembezi, anyamuka m'dziko muno mawa kupita ku South Africa.
Chembezi akukayesa mwayi ku timu ya Polakwane City m'dziko-lo.
Savenda Chitipa United will commence 2020 football preparations in February.
One of the club's senior official, Pickford Kamanga has confirmed the development to Owinna.
Malawi National Council for Sports will on 14 February hold the 2019 Malawi National Sports Awards in Lilongwe.
This has been confirmed by Sports Council officials.
Schumacher Kuwali is set to join UD Songo, a club based in Mozambique.
Chairperson for Blue Eagles, Alexandar Ngwala, has confirmed the development.
Civil Sporting has released some of its players due to performance, transfers and who were on loan.
Emmanuel Zoya has resigned from active football following his new post at Civil Sporting.
Zoya has been offered a position in the club's technical panel.
Sports Commentators have pleaded with FAM to reconsider it's decision of introducing minimum salaries of players for teams to follow.
According to the people who have talked to Owinna, it's hard to follow the initiative because of the current economic hardships.
Matimu komanso osewera omwe anachita bwino mu mpikisano wa FISD akuyenera kudikirabe kuti adziwe tsiku lomwe azalandire mphoto zawo.
Akuluakulu omwe amayendetsa mpikisano-wu sananene za tsikuli.
Flames Coach, Meke Mwase, is yet to sign his 1 year contract after heading the coaching panel for about 7 months.
According to confirmed reports, contract for Mwase is now ready for signing.
Fischer Kondowe walangiza osewera anzake kuti achirimike pa okha pa nthawi yomwe matimu awo akupuma kuti ayambe zokonzekera za 2020.
Kondowe wanena izi mu kanema yemwe watulutsa posachedwapa.
Liverpool star, Sadio Mane, has won the African Player of the year award.
The award is for 2019.
1
Kamuzu Barracks player, Chikoti Chirwa, is set to leave today for South Africa.
According to reports, Chirwa is expected to undergo trials at Amazulu.
Timu ya Nyasa Big Bullets yati ikhala ndi mwambo wopereka mphoto kwa osewera omwe anachita bwino mu 2019.
Mmodzi wa akuluakulu a timuyi, Albert Chigoga, watsimikiza za nkhaniyi.
Chawanangwa Kaonga has joined TS Sporting on a 2 year contract from Costa do Sol.
The club is based in South Africa.
Kaonga last year helped Costa do Sol lift a trophy by scoring crucial goals.
Wosewera kutsogolo kwa timu ya dziko lino, Gabadinho Mhango, akutsogola ndi zigoli mu ligi yaikulu ku South Africa.
Izi zikutsaira kumwetsa zigoli zitatu kwa katswiri-yu m'masewero a timu yake.
Deadly Gabadinho Mhango yesterday scored a hat trick for Orlando Pirates to help his team beat Polakwane City 4-1.
Mhango was also voted as Man of the Match (MOTM).
Wapampando wa masapota wa timu ya Wanderers, Melvin Nkunika, wati apikisana nawo pa chisankho chomwe chichitike ku timuyi posachedwapa.
Kumathero a chaka chatha a Nkunika anati sapikisana nawo.
Ndipo mlembi wa masapota wa timuyi wati apikisana nawo pa chisankho-chi.
Timu ya Wanderers yati yapeza chifukwa chomwe chimapangitsa kuti adzikhala ndi ngongole zochuluka chaka chili chonse.
Wapampando wa masapota wa timuyi, Melvin Nkunika, ndiye wanena izi.
A Nkunika ati kukhala ndi osewera ochuluka ndikumawapatsa malipiro apa mwezi ndi chinthu chimodzi chikuchititsa izi.
BE FORWARD Wanderers midfielder, Francisco Madinga, will today fly to Georgia.
According to confirmed reports, Madinga has been offered a 2 year contract by FC Dila Gori.
FC Dila Gori plays in the top flight league in Georgia.
Super League of Malawi (Sulom) will release 2019 TNM Super League financial report in March this year.
Sulom General Secretary, Williams Banda, has confirmed the development to Owinna.
Gulu la MBC Stand Supporters Initiative lati likufuna liyambe kugwira ntchito ndi mabungwe a FAM komanso Sulom pofuna kukwaniritsa zokhumba zake potukula masewero a mpira m'dziko muno.
Mlembi wa gulu-li, Charles Mangani, ndiye wanena izi.
Muhammad Sulumba will this year play for a yet to be named club in Vietnam. The former Nyasa Big Bullets player, who scored 10 goals for Civil Sporting last season, left for Vietnam yesterday.
Flames striker, Gabadinho Mhango, has scored 7 goals for Orlando Pirates in South Africa.
Mhango is on position 7 with a difference of 2 goals from Peter Shalulile who is topping the scorers list.
Super League of Malawi (Sulom) Vice President, Gilbert Mitawa, will be the body's legal advisor on temporary basis. General Secretar for Sulom, Williams Banda, has confirmed the development to Owinna.
Wapampando wa timu ya BE FORWARD Wanderers, Gift Mkandawire, wabwereza kuti saima nawo pa chisankho cha timuyi. A Mkandawire anena izi pomwe apempha kuti komiti yoyendetsa chisankho ikhazikitsidwe.