Login with Facebook to post predictions, updates & live scores
Fischer Kondowe wati timu yomwe ayambe kusewera masewero akayambiranso ikhala ndi mwayi waukulu otenga chimodzi mwa zikho zomwe zimakhalapo mdziko muno.
Fischer Kondowe has been appointed as Nyasa Big Bullets second assistant coach.
This comes after the player announced that in 2020 season he will not play active football.
Osewera wakale wa Nyasa Big Bullets, Fischer Kondowe, wati akulingalirabe zoti achite kutsatira kuuzidwa ndi akuluakulu a timuyi kuti asiye mpira.
Amid pressure from Nyasa Big Bullets officials, Fischer Kondowe, last month announced that he has retired from active football pending a job offer at the club.
Fischer Kondowe ati wachita kupangilidwa chiganizo kuti asiye kusewelera ku Bullets pomwe timuyi inalibe chidwi choonjezera kontrakiti yake.
Fischer Kondowe walangiza osewera anzake kuti achirimike pa okha pa nthawi yomwe matimu awo akupuma kuti ayambe zokonzekera za 2020.
Kondowe wanena izi mu kanema yemwe watulutsa posachedwapa.
Flames Greats to play on Wednesday during Gianni Infantino visit to Malawi.
The team includes; Patrick Mabedi, Joseph Kamwendo, Fischer Kondowe, Chancy Gondwe and Swadick Sanudi.
Fischer Kondowe has admitted to lacking some discipline being a senior player.
In his Facebook post, Kondowe says he will serve his suspension and return a changed coach player.
Nyasa Big Bullets has suspended long serving player for the club, Fischer Kondowe.
According to confirmed reports the player has been suspended for a month.
How come we missed this? Happy belated birthday Fischer Kondowe. He is now 38.
Happy belated Birthday Anong'a!
Osewera mu timu ya Bullets, Fischer Kondowe, wati siokhumudwa kuti anthu okonda timuyi sanamusankhe pa chisankho chapatatu.
Fischer wanena izi pomwe zotsatira zotsatsimikiza zaonetsa waluza
Fischer Kondowe (NBB) to continue active football while contesting for MP for Blantyre City South against Peter Mponda (PBW) and other politicians. malawi24.com
FT: Nyasa Big Bullets 5 - 1 MTV Max Bullets (Mussah Manyenje, 2x Chiukepo Msowoya, Fischer Kondowe, Macfarlen Mgwira - Tonu Biasi)
FT: Nyasa Big Bullets 5 - 1 MTV Max Bullets (Mussa Manyenje, 2x Chiukepo Msowoya, Fisher Kondowe, McFaren Mgwira - ?)
FT: Big Bullets 2 - 1 Civo United (Fischer Kondowe, Yamikani Fodya - Nelson Kangunje)
FT: Big Bullets 4 - 1 Chikwawa United (2x Fischer Kondowe, Mussah Manyenje - John Banda, Jimmy Zakazaka)
FT: Big Bullets 2 - 1 Kamuzu Barracks (Sankhani Nyirenda, Fischer Kondowe - Harvey Mkacha)
FT: Kamuzu Barracks 1 - 1 Big Bullets (Fisher Kondowe)
FT: Escom United 1 - 5 Big Bullets ((OG) Chikumbutso Kanyenda - Fisher Kondowe, Gabadinho Mhango, Divason Mlozi, James Chilapondwa, Dalitso Sailesi)
FT: Big Bullets 1 - 1 Blantyre United (89' (P) Fisher Kondowe - 51' Sparrow Msowoya)