Mphunzitsi wa timu ya Flames, Meck Mwase, wati pakadali pano palibe dongosolo lomwe waika lofuna kuti osewera azipitilira kuchita zokonzekera pakati pa mliri wa Covid-19.
Koma waalimbikitsa osewera kuti adzichita zokonzekera pawokha. Zofunika 👍⚽
Login with Facebook to post predictions, updates & live scores