Timu ya Wanderers yasainirana mgwirizano watsopano ndi kampani ya BE FORWARD yomwe imathandiza timu-yi.
Mmodzi mwa akuluakulu ku Wanderers, Mike Butao wati asainirana mgwirizano wa zaka zitatu.
Login with Facebook to post predictions, updates & live scores