Nkhani
Timu ya Mighty Wanderers yatsimikiza kuti Bob Mpinganjira ndiye atsogolere timuyi mu ligi ya chaka cha 2025.
Mpinganjira wasaina mgwirizano wa chaka chimodzi kutsimikiza tsopano kuti si ogwiriziranso ayi koma wokhazikika.
Login with Facebook to post predictions, updates & live scores