NKHANI
Mkulu oyang'ana za club licensing ku bungwe la Football Association of Malawi, Cassper Jangale, walembera kalata bungweli yoti akufuna kusiya ntchito atagwirako kwa zaka 19 kuchokera mu 2005.
Izi ndi malingana ndi zomwe nyuzipepala ya Nation ya mtsiku la lero yalemba.
Login with Facebook to post predictions, updates & live scores