Katswiri wakale wa Silver Strikers, Adiel Kaduya, waziyambitsa kale ku Masters Athletics mdziko la USA.
Iye wati ndi wokondwa poti wayamba ntchito yake ya m'bwalo la zamasewero ndipo akuyembekezera kusewera masewero ochuluka kwambiri ndi timuyi.
Iyeyu akusewera timuyi yomwe ndi ya sukulu yaukachenjede ya Masters University mdzikoli komwe akukapitiliza maphunziro ake.
Mutumize pa nanba iyi 0991509953
Login with Facebook to post predictions, updates & live scores