Ndime yoyamba yampikisano wa TNM itha sabata ino ndi masewero asanu omwe bungwe la Super League of Malawi (Sulom) laika.
Matimu a Blue Eagles, Dedza Dynamos, MAFCO komanso Karonga United ndi ena omwe akusewera masewero awo omaliza.
Timu ya Nyasa Big Bullets imaliza panambala 1 ndi mapoint 41 pa masewero 15 omwe yasewera mundime yoyambayi.
Login with Facebook to post predictions, updates & live scores