Timu ya Silver Strikers yatulutsa jeze yatsopano yomwe akhale akugwilitsa ntchito sizoni ino.
Malingana ndi kalabu-yi, Jeze-yi iyamba kugulitsidwa posachedwapa mzigawo zonse za dziko lino.
Silver Strikers yati izigulitsa Jeze-yi K20, 000.
Login with Facebook to post predictions, updates & live scores