Mtsogoleri wa bungwe la FAM, Walter Nyamilandu, wapempha anthu okonda masewero kuti adekhe pomwe ati amaliza ndondomeko zonse zoyenereza masewero kuyamba mdziko muno.
Login with Facebook to post predictions, updates & live scores