Login with Facebook to post predictions, updates & live scores
Azantu akaronga zimachitika pepani
a fam ziphuphu kwambili olakwitsa ndi Ref chilango kupita ku team chitan manyazi.
Silvar straiks mumatimvetsa kukoma mpila nkumwendo koma esetsani,a b,lets, atikakata mafuno abwino.
Big up ma Bankers
Karonga vs silver
Nyasa big bullets fc
Timu ya Silver Strikers ili m'chigawo cha kumpoto komwe isewere ndi matimu a Chitipa United komanso Karonga United mu ligi ya TNM.
Timuyi isananyamuke mu mzinda wa Lilongwe inali ndi mwambo wa mapephero komwe kunamwera mtumiki wa mulungu kuzacheza nawo.
Silver Strikers mu ndime yachiwiri yampikisano wa TNM sinawineko masewero ali onse pa masewero atatu omwe yasewera.
Malawi football updates
B.b wanobe nobe kut buu ANT GIRE
Nhassa Big bulles hoye 45 poit
Update
MWANA NDIMWANA BASI
GO A HEAD NYERERE
Ntopwa ija yapita m'chigawo chapakati komwe isewere ndi matimu a MAFCO komanso Blue Eagles mu ligi ya TNM.
Kampani ya Energem Petroleum Limited ndiyo yawathandiza ndi mafuta omwe agwiritsa ntchito pa ulendo-wu.
Mkulu wa aphunzitsi a Ntopwa yemwenso ndi mwini wake, Isaac Jomo Osman, posachedwapa anatsindika kuti sapita m'chigawo chapakati akapanda kupeza thandizo.
Timu ya Karonga United yati mayere omwe achitika mu mpikisano wa FDH Bank aphelezera zofuna zawo.
Mmodzi mwa aphunzitsi a timuyi, Dan Dzinkambani, wanena izi pamene asewere ndi Wanderers.
Transfer how is it lurs niw
Kodi game yanj ionetsedwe this coming sunday
Kodi game tionera tv yanj
World Vision Malawi donates 207 balls to Mchinji schools
World Vision International Malawi on Wednesday donated 207
World Vision International Malawi on Wednesday donated 207 footballs to Primary and Secondary Schools in Mchinji.
Mereena John, World Vision Manager for Mchinji said the donation will help the youths in the district to actively participate in sports developmental activities taking place in the area.
According to John, World Vision want primary and secondary schools to be the hub of producing stars for Super League teams.
World Vision International Malawi is implementing developmental projects in Mchinji.
Ntopwa are now winless in 12 Super League games following a humiliating loss to Nyasa Big Bullets on Wednesday.
In 12 matches, Ntopwa has now 10 defeats and 2 draws.
Pepan akaronga zimachitika
[image]
Mkulu wa aphunzitsi ku timu ya Ntopwa yemwenso ndi mwini wake, Isaac Jomo Osman, wati boma pamodzi ndi mabungwe a Sulom komanso FAM akuthandizira kuti timuyi ituluke mu ligi yaikulu mdziko muno, TNM.
A Osman anena izi patsogolo pa masewero omwe apatsidwa m'chigawo chapakati pamene asewere ndi matimu a MAFCO komanso Blue Eagles kumathero a sabata ino.
Iwo ati alibe ndalama zoti agwiritse ntchito pa ulendo wawo okasewera masewero amu ligi ya TNM m'chigawo chapakati.
Mkulu wa Ntopwa-yu wati ngati sapeza thandizo wazisiya ndipo Sulom ipereke mapoint ku matimu omwe asewere ndi Ntopwa kumathero a sabatayi.
Nyasa Big Bullets hit-man, Hassan Kajoke, has now scored 10 goals in the country's top tier league following Wednesday's hat-trick against Ntopwa.
zofunikila ndizimenezo neba mutu siukugwila
Kod akutsogola zigori ndindani pakati pa kajoke ndi phodo nanga zigori zawo zili motani?
Kkkkkkkkkk maule pa top basi kmaso prediction yanga ya 3-0 yathekatu ndinanena dzana
More drama in TNM Super League week-in, week-out.
On Saturday Ekwendeni were winners over Tigers 1-0, Blue Eagles beat MAFCO 1-0 and Silver Strikers drew with KB 0-0.
Teams like Ekwendeni, Karonga, Chitipa & TN Stars are doing better since for them to walk away with a point it's a bonus. They play to be in the league, so they play without pressure and get results.
To win be champions it's a nightmare. Time is running out and pressure is with Silver & Bullets. Nomads, a little. Due to this pressure, Silver is doing things in a hurry and results are not coming.
They could have won the league in the first round when they opened a 5 point gap plus a game in hand. Now itβs one.
Letβs wait and see. Tough and very tough indeed. Pa ground pavuta.
This weekend draw on fdh
Maule for life β½οΈπ