Ntopwa ija yapita m'chigawo chapakati komwe isewere ndi matimu a MAFCO komanso Blue Eagles mu ligi ya TNM.
Kampani ya Energem Petroleum Limited ndiyo yawathandiza ndi mafuta omwe agwiritsa ntchito pa ulendo-wu.
Mkulu wa aphunzitsi a Ntopwa yemwenso ndi mwini wake, Isaac Jomo Osman, posachedwapa anatsindika kuti sapita m'chigawo chapakati akapanda kupeza thandizo.
Login with Facebook to post predictions, updates & live scores