FLAMES NDI 123 NDI NGANGANGA
Timu ya Flames ikadali pa nambala 123 pa ndandanda wa matimu onse pa dziko la pansi kutsatira ndi ndandanda omwe bungwe la FIFA latulutsa lachinayi.
Mu ndandandawu, Malawi sinasuntheko tsopano kws mwezi wachitatu wolumikiza ndipo izi zili chomwechi kamba koti sanamenyeko mpira uliwonse mwezi wa October.
Timuyi tsopano ili pa nambala 33 mu Africa komanso ili pa nambala yachisanu ndi chiwiri (7) kummwera kwa Africa uno. Umu ndi mmene zilili.
1️⃣12. South Africa (64) 2️⃣16. Zambia (81) 3️⃣23. Madagascar (108) 4️⃣26. Mozambique (113) 5️⃣27. Namibia (114) 6️⃣28. Angola (116) 7️⃣33. Malawi (123) 8️⃣34. Zimbabwe (125) 9️⃣37. Comoros (128) 1️⃣0️⃣43. Eswatini (146) 1️⃣1️⃣44. Botswana (148) 1️⃣2️⃣46. Lesotho (153) 1️⃣3️⃣48. Mauritius (177) 1️⃣4️⃣52. Seychelles (195)
Wolemba: Hastings Wadza Kasonga Jr
Login with Facebook to post predictions, updates & live scores