Khuda Muyaba apitilira kumwetsa zigoli ku Joni
Katswiri wa timu ya Polokwane City Khuda Muyaba Lamulungu anagoletsa chigoli pamene timu yake yaluza, 3-1 ndi timu ya Uthangothi.
Ichi ndi chigoli cha nambala 7 cha Khuda Muyaba mu mpikisano wa Glad Africa Championship.
Padakali pano katswiriyu akutsogola ndi zigoli mu mpikisanowu.
Polokwane City sabata ya mawa isewera ndi TS Sporting pa bwalo la Kabokweni.
Login with Facebook to post predictions, updates & live scores