Nduna ya achinyamata ndi masewero, Ulemu Msungama, yabwereza kuti siyokhutira ndi momwe mtsogoleri wa FAM akugwirira ntchito yake pomwe akumatenga mbali yaikulu pa nkhani za ndale.
Login with Facebook to post predictions, updates & live scores