Katswiri wotchinga pa golo, Brighton Munthali, wamvana ndi timu ya Masters Security kuti akakhale kutimuyi mu mgwirizano wa zaka ziwiri.
Izi zadza pomwe masiku apitawa wathetsa mgwirizano wake ndi Creck Sporting Club kamba kosasewera pafupipafupi.
Login with Facebook to post predictions, updates & live scores