Timu yomwe yagula umwini wa Baka City ya Masters Security ikufuna kutenga Steve Madeira kukhala mmodzi wa aphunzitsi a timuyi.
Madeira anadziwika bwino pokhala timu maneja wa Mighty Wanderers ndi Bangwe All Stars koma padakali pano alibe timu.
Login with Facebook to post predictions, updates & live scores