NKHANI
Timu ya Creck Sporting Club ikumana ndi timu ya Ntcheu Select pa masewero omwe akhaleko pomwe mtsogoleri wa dziko lino Dr Lazarus Mccarthy Chakwera akhale akutsegulira bwalo la Ntcheu lero.
Timuyi yatsimikiza za izi kudzera pa tsamba lake la mchezo la Facebook ndipo yati ikunyamuka ku Lilongwe kutsikira mu boma lokometsetsa Malawi yonse ino.
Login with Facebook to post predictions, updates & live scores