Timu ya Ekhaya FC ikupitilirabe kulimbitsa timu yawo pomwe yasaina katswiri wa pakati kutimu ya Civil Service United, Moses Banda.
Timuyi yatsimikiza za izi kudzera pa tsamba lawo la mchezo lachitatu.
Login with Facebook to post predictions, updates & live scores