Timu ya FCB Nyasa Big Bullets tsopano lero yachita zokonzekera zawo pa bwalo la Chitipa poti khonsolo ya Boma la Chitipa yavomera pempho lawo losewerera pa bwaloli.
Dzulo timuyi inakanizidwa kupanga zokonzekera pa bwaloli ndipo anachita kusaka bwalo lina kuti apangirepo zokonzekera zawo.
Login with Facebook to post predictions, updates & live scores