Timu ya Creck Sporting Club yalekana ndi katswiri wawo Isaac Msiska yemwe wachoka kutimuyi Kamba kosowa mpata wosewerasewera.
Iye anapita kutimuyi itatha ligi ya chaka chatha kuchokera ku Mzuzu City Hammers komwe anagoletsa zigoli 12 mu 2024.
Login with Facebook to post predictions, updates & live scores