Timu ya Creck Sporting Club yatsimikiza kuti yatenga katswiri wosewera pakati kutimu ya Silver Strikers, Patrick Macheso, yemwe wapita kutimuyi pa ngongole.
Iye wapita kutimuyi kutsatira kusowa nthawi yosewera kutimuyi pomwe sanasewereko masewero angakhale amodzi pansi pa Mphunzitsi Peter Mgangira.
Login with Facebook to post predictions, updates & live scores