Bungwe la Super League of Malawi lati msika wogula ndi wogulitsa osewera watsegulidwa usiku wa pa 31 July 2024 ndipotu udzatsekedwa pa 09 August 2024.
Mu kalata yomwe yasainidwa ndi mlembi wabungweli, Williams Banda, yati bungweli likhale likuyang'ana mmene matimu azipangira malonda awo cholinga pasapezeke zitopotopo zina ndi zina.
Login with Facebook to post predictions, updates & live scores