Moni nose okonda masewelo amulosela pano pa owinna.com. Malingana ndinkumano omwe unali lero omwe timachezana kudzela pa WhatsApp komaso pa kuimba foni. kwamene sitinakwanise kucheza nanu pankumanowu tagwilizana kuti kuyambila loremba pa 24 August pasapezekeso olosera masewero aliwose m'paka kufikila atapeleka m'photo zose kuyambila sabata yothela 26 July m'paka sabata ino yothela 23 august 2026. Izi tagwilizana chifukwa chakukaikila komwe kulipo posalandila mphotozi kuti mwina ndikutseka kwa page ya owinna.com koma safuna kutitsikimizila admin wathu. ZIKOMO OLOSERA NOSE.
Good. I'm very happy for this meeting. Zilibwino akutinamizadi
Login with Facebook to post predictions, updates & live scores