Timu ya Wanderers yati ipereka chili chonse choyenera kwa Babatunde Adepoju kuti athandize timuyi kuchita bwino mu mipikisano ya 2020.

Mlembi wa Nyerere, Victor Maunde, watsimikiza za nkhaniyi.

19 May 07:39

Share on Facebook
Post Predictions & Updates

Login with Facebook to post predictions, updates & live scores