NKHANI
Timu ya Bangwe All Stars yayimitsa wachiwiri kwa mphunzitsi wa timuyi Davie Matemba kamba ka kusachita bwino kwa timuyi.
Matemba wayimitsidwa kamba koti ndi amene wakhalitsa kwambiri ndi timuyi makamaka mu masewero akoyenda omwe mphunzitsi wamkulu Isaac Jomo Osman samapezekako.
Timuyi inapambanako kamodzi kokha mu ligi ndi kufananitsa mphamvu katatu pa masewero 13 omwe asewera.
Login with Facebook to post predictions, updates & live scores