Login with Facebook to post predictions, updates & live scores
Wakhala ndiakamuna kuti agoretse ababatunde
Nyasa bb vs sable bwanji
2:0
Iminiti ipi?
FDH knockout
Sabble faming vs nyasa big bullets
mighty tigers 0 nyasa big bullets res 1
Yatha bwanji pano pama penalty?
We lobe nomads
Timu ya Silver Strikers yatuluka mumpikisano wa FDH Bank kutsatira kugonja ndi Dedza Dynamos Salima Sugar 5-4 pa mapenate.
Masewero-wa anathera 0-0 muphindi 90.
Zateremu, timu ya Dedza Dynamos yafika mundime ya matimu 16.
Patrick Mwaungulu wasankhidwa kukhala wosewera yemwe anasewera bwino kuposa anzake onse ku timu ya Nyasa Big Bullets m'mwezi wa June.
Timu ya Nyasa Nyasa Big Bullets yatsimikiza za nkhaniyi.
Mwaungulu amapikisana ndi Babatunde Adepoju komanso Chimwemwe Idana.
Chigoli chomwe Gabadihno Mhango anagoletsa pamene timu ya Malawi imasewera ndi Morocco m'mpikisano wa AFCON achisankha kuti chipikisane nawo pa chigoli chapamwamba cha chaka chino.
Bungwe la CAF latulutsa kanema wa zigoli zomwe zikupikisana nawo pa mphoto-yi.
@Gabadinho mhango
Isaac, Aquila & Mark agawana K10,000πΈ atalosera molondolaπ― magemu atatu kuposa ena onse sabata yatha pa owinna.comβ½
The Confederation of African Football (CAF) on Tuesday confirmed that the Flames are through to the second round of the 2022 Chan qualifiers without kicking a ball.
This follows the failure of Zimbabwe to get their FIFA suspension lifted.
Malawi was drawn against Zimbabwe in the first round of the qualifiers.
However CAF Indicated that the fixture will go ahead only if Zimbabweβs FIFA suspension is lifted two weeks before the first match which was scheduled for July 23, 2022.
A letter from CAF to FAM has confirmed the development.
Ss
2022 Chipiku stores and football