Login with Facebook to post predictions, updates & live scores
Noma the giant of Malawi
Apolisi anagwiritsa ntchito utsi okhetsa misonzi pobalalitsa anthu ena omwe amalowa ku bwalo la Mulanje Park pogwiritsa mpanda.
tnm supa lig
Orlando Pirates on Saturday defeated Celtic, 3-1.
Gabadhno Mhango scored the third goal after coming in as a substitute.
Northern Region Football Association (NRFA) has endorsed James Mwenda for Football Association of Malawi (FAM) Presidency.
FAM is expected to hold the elections in December this year.
Log table
Bullets simaphweketsa
Nyasa Big bullets vs Silver strikers
Joseph Kamwendo wamaliza maphunziro a uphunzitsi omwe amatenga nawo mbali.
Kamwendo wamaliza maphunziro-wa Lachinayi.
Maphunziro-wa anali olingana ndi CAF C. Licence.
Kamuzu Barracks ili ndi mwayi okhala patsogolo wa ndandanda wa matimu amu TNM ngati atambana masewero awo lero.
Kamuzu Barracks ikusewera ndi timu ya Civil Sporting.
Chigawo cha chiwiri cha masewero amu ThumbsUp chiyamba pa 17 August.
Mmodzi wa akuluakulu oyendetsa ligi-yi, Kingsley Simbeyi, wauza izi Owinna.
Fixtures
Bungwe la FAM lero litulutsa ndandanda wa maina wa osewera a chisodzera.
Osewera-wa akuyembekezeka kuyamba kuchita zokonzekera Lolemba likudza-li.
Mwini wake wa timu ya Masters Security, Alfred Gangata, wati osewera a timuyi ndiwo akuyenera kupanga chiganizo ngati akatenge nawo mbali ku mpikisano wa CAF. Gangata wati zonse zofunikira wamaliza.
Alick Harawa, osewera wa Rumphi United ndiye akutsogola ndi zigoli mu ligi ya SIMSO.
Osewera-yu wamwetsa zigoli 12 pakadali pano.
Timu ya Red Lions yamaliza chigawo choyamba cha ThumbsUp Premier Division pa namba 1.
Pa masewero 19 omwe timuyi yasewera yapeza mapoint 50 ndipo yachiwiri ndi timu ya Sable Farming ndi mapoint 42.
BB 1 - BANKER 4
eni #nkaka
Mphunzitsi wa Wanderers, Osacar Kaunda, wati zokonzekera za timuyi zikuyenda bwino.
Kaunda wati osewera akuchirimika pomwe pali mpikisano waukulu pakati pa osewera.
Osewera achisodzera 40 omwe asakhidwa Lolemba omwe atenge nawo mbali mu mpikisano wa COSAFA Youth Champion akuyembekezeka kuyamba kuchita zokonzekera zawo pa 5 August.
Timu ya Ntopwa yati sidya fulumira posankha mphunzitsi watsopano wa timuyi kutsatira kusiya kwa Leo Mpulula.
Isaac Osman wati timuyi ipeza mphunzitsi wa tsopano ndime yoyamba ya TNM ikatha.
Khuda on it again!! Jokes about Babatunde.
Muyaba is optimistic of winning TNM top goal scorer award.
Whilst Babatunde says Khuda has made the call early.
Leo Mpulula wasiya kuphunzitsa timu ya Ntopwa kutsatira kugonja kwa timuyi dzulo ndi Tigers.
Mpulula sananene zifukwa zomwe wasiyira ntchito.
Soccer fans in the country attribute poor turnout in yesterday's game of Mighty Tigers vs Ntopwa to Blantyre Derby results.
First round of SIMSO Premier League is expected to come to an end in August.
According to Ollens Msonda everything is going as planned.
TN Stars yesterday missed a chance of topping TNM Super League following Silver Strikers defeat.
The bankers won the game 2-1.
Meanwhile Wanderers is leading with 27 points.
Akuluakulu oyendetsa ligi ya kumwera ati ndi okhutira ndi momwe ligi-yi ikuyendera.
Izi zikutsatira kutha kwa ndime yoyamba ya mpikisano wa ThumbsUp Lamulungu.