Login with Facebook to post predictions, updates & live scores
Nyelele Patsogolo
TNM log table
1-1
Tn 1-1 Silver
DEVES MEDJA MEDJA
Civo 0-0 Blue Eagles
36 million Kwacha ndi ndalama zapangidwa pa masewero a dzulo apakati pa Bullets ndi Wanderers.
bullets_1-2_silver
BB 0 0 noma
Live Nyasa big bullets vs Befoward wanderes
chipiku premier fixtures
Chipiku Premier Division & Division 1 fixtures updated.
Akuluakulu oyendetsa mpikisano wa ThumbsUp ati ndi okhutira ndi momwe mpikisano-wu ukuyendera.
Kingsley Simbeyi, wanena izi kutsatira kutha kwa ndime yoyamba ya mpikisano wa Division One.
Yadyedwanso wanderers ija
bforwards nditeam yomwe imandivetsa kukoma kwambri rather than else!
2
Bullets oye
Bungwe loyendetsa masewero mdziko muno la, FAM, lichititsa masewero a matimu a chisodzera a zigawo.
Iyi ndi njira yomwe agwiritse ntchito posankha osewera a timu ya dziko lino ya chisodzera.
Mphunzitsi wa Flames, Meke Mwase, akuyendera matimu onse amu Super League pomwe akupeza osewera a timu ya dziko lino-yi.
Mwase sabata ino ali m'chigawo cha kumpoto.
Team Manager wa timu ya Wanderers, Victor Maunde, wati osewera akonzeka kusintha mbiri Loweluka.
Maunde wati patadutsa zaka 6 asanagonjetse Bullets mu ligi uwu ndi mwayi wawo.
John Lanjesi komanso Miracle Gabeya ayamba kuchita zokonzekera ndi timu ya Bullets.
Awiri-wa anali ovulala sabata zingapo zapitazo.
Pali mwati oti awiri-wa atha kupezeka pa masewero a Loweluka.
silver strikers vs noma
Antony
Titaona kuti tilipati
silver strikers vs be foreward wonderers
Nzuni 2-0 Dwanga
Chitipa 0-0 Moyale
Mmodzi wa akuluakulu a BE FORWARD Wanderers, Gift Mkandawire, wati masapota a timuyi adekhe ponena kuti chili chonse ku timuyi chikuyenda bwino.
Daby yomwe ikubwerayi ndiyovuta kuneneratu kamba koti ma team onsewa ali ndi osewera abwino komanso amadziwana matseweredwe koma ine ndikupeleka mwayi ku team ya wanderers kuti ikhoza kupambana
Tikamapanga chili chonsecho tisaiwale kuti kumathero kwa sabata ino, Loweluka likudza-li kuli Blantyre Derby.
Joseph Kamwendo sabata ino akhale akutenga nawo mbali pa maphunziro a uphunzitsi mu mzinda wa Blantyre.
Kamwendo wayamba maphunziro-wa dzulo ku sukulu ya St Andrews.
Mphunzitsi wa timu ya Nyasa Big Reserve, Enos Chatama, wati season ino sakufuna kulimbirana nawo ukatswiri wa ThumbsUp Premier Division omwe anapambana chaka chatha.
Boa pensamento
Peter Mponda tsopano ndi wachiwiri kwa mphunzitsi wa timu ya Nyasa Big Bullets.
Mponda wayamba ntchito yake dzulo pomwe anaonekere ku timuyi.
Mphunzitsi-yu mbuyomu anasewerako timuyi.
Help me with chipiku stores premier division fixtures
nyasa bullets 0-Be forward wonderes 1
Red Lions coach, Nelson Chirwa, says if the team maintains current form will return in the elite league next season.
Chirwa said this following Sunday's win against Nyasa Big Bullets Reserves.
One of Nyasa Big Bullets supporters on Sunday gave Hassan Kajoke a chicken as one way of appreciating the young stars efforts.