Mmodzi wa akuluakulu a BE FORWARD Wanderers, Gift Mkandawire, wati masapota a timuyi adekhe ponena kuti chili chonse ku timuyi chikuyenda bwino.
Daby yomwe ikubwerayi ndiyovuta kuneneratu kamba koti ma team onsewa ali ndi osewera abwino komanso amadziwana matseweredwe koma ine ndikupeleka mwayi ku team ya wanderers kuti ikhoza kupambana
Login with Facebook to post predictions, updates & live scores