Kod ku sliver zikut bwanji guss
Pankhani yanji ku Silver ko?
ma transfers akuyenda bwanji
Timu ya Silver Strikers yasaina Sheriff Shamama wa Karonga United ndipo osewera ena monga Muhammad Sulumba ndi ena akunja ochokera ku Nigeria ndi Cameroon nawo akuyetsa mwai ku mabankers
Bullets ndi Noma amaliza kugula osewera. Bullets yagula Precious Sambani, Luke Chima ndipo Noma yagula Peter Katsonga kungotchula ochepa
Login with Facebook to post predictions, updates & live scores