Katswiri womwetsa zigoli ku timu ya Silver Strikers, Binwell Katinji walemba kalata yotsanzika kutimuyi pomwe akuchokako.
Iye watulutsa kalatayi lachinayi yomwe wathokoza akuluakulu a timuyi pokhala naye ndi aphunzitsi pomukhulupilira ku timuyi.
Katinji sananene komwe akulowera koma mphekesera zikuonetsa kuti akupita mdziko la Zimbabwe komwe kwapita osewera aku Malawi ochuluka.
Login with Facebook to post predictions, updates & live scores